George Bonomali

George Bonomali Christ’s | sign language | special needs | early childhood

Went to Kwanjana today 😅
15/08/2025

Went to Kwanjana today 😅

Look at this!Spend good quality time in the Word at Zomba mountain from Friday to Sunday (3-5 October 2025).Register wit...
15/08/2025

Look at this!

Spend good quality time in the Word at Zomba mountain from Friday to Sunday (3-5 October 2025).

Register with just MK5,000 then boom, all expenses covered!! For university/college students from southern region.

Varsity Fellowship of Malawi has been at it for over 5 years.

More details on their page and this flyer.

11/08/2025

It’s a good thing we don’t see the future. Coz we’d ruin it every chance we get.

The name “Lilongwe” means what in Chichewa?a) Place of baobab treesb) Place of tonguewe treesc) Place of reedsd) Place o...
10/08/2025

The name “Lilongwe” means what in Chichewa?
a) Place of baobab trees
b) Place of tonguewe trees
c) Place of reeds
d) Place of rivers

Kodi mukudziwa kuti pali ulumali wina otchedwa Deafblindness?Muthu yemweyo wa deaf komanso wa blind.Alipo anthu ena omwe...
09/08/2025

Kodi mukudziwa kuti pali ulumali wina otchedwa Deafblindness?

Muthu yemweyo wa deaf komanso wa blind.

Alipo anthu ena omwe deafness yawo imakhala ya pang’ono kapenanso blindness yawo ya pang’ono. Olo pena chimodzi kukhala cha pang’ono kuposa chinzake.

Anthuwa amalemba ndi kuwerenga kudzera mu njira ya braille olo kudzera mu njira ya ngati inu ndi ine, koma zimatengera kukula kwa kusawona kwawo.

Kayankhulidwe kawo kamakhala mu njira ya tactile sign language olo sign language yomweyi kutengera level ya deafness yawo.

Nde pali ena oti amakhala ndi complete Deafblindness. No sight, and no hearing.

Za kaphunzitsidwe kawo nde musanene. Imakhalako.

Alamwanu ndi amenewo 😅🤟
07/08/2025

Alamwanu ndi amenewo 😅🤟

Last week kunali graduation ku For a Change ndipo Max & Sherry Dine and Lounge inabwera kudzatipanga chi surprise by GM ...
28/07/2025

Last week kunali graduation ku For a Change ndipo Max & Sherry Dine and Lounge inabwera kudzatipanga chi surprise by GM Plastics Industry LTD. Kubwera kwao kunabebetsa gala osati masewera!! Komanso getting mentioned in the same breath with these names is a huge honor. Thank you a million times for the recognition and your donation to the center.

27/07/2025

Mwina tizingopanga compare ma results a mwana a term yatha ndi term ino. Kenako tione pomwe asakuchita bwino kuti term ya mawa tidzamuthandize. Izi zakuti uyu ndi number 1, uyu chimtseka khomo sizimapindula kwenikweni makamaka kwa ana omwe kuti school imawavutirako.

27/07/2025

Nkhani ndi yoti alipotu anthu oti sanakhalepo number 1 nkalasi koma pano zawo zili pabwino kuposa omwe amachita bwino nkalasi.

27/07/2025

Week yangothayi ndinamva mayi wina akuti, “iih awaposatu ulendo uno, akhala number 4”.

Ka mnyamata kanangoyima ndwii kusowa choyankha.

Mukuwona ngati mwanayo anali motivated kuti next term adzalimbikire?

27/07/2025

Ana atsekera sukulu, koma ine ndili ndi funso. Zomawayika ana kuti uyu ndi number 1, uyu chimtseka khomo mukuona ngati zimathandiza ophunzira?

Kodi ma advantages ndi ma disadvantages ake ndi otani?

26/07/2025

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when George Bonomali posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to George Bonomali:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram