The health Hub

The health Hub Raising awareness on healthy habits and disease insights.

The health hub ikukuonanitu!Simukumwa madzi kumeneko..Alex Mbendera
20/09/2025

The health hub ikukuonanitu!
Simukumwa madzi kumeneko..

Alex Mbendera

Muli ndi kuthekera kokudya zakudya zakasinthasintha? Musanyalanyaze kuchita motero. Zindikirani kuti zakudya zosiyanasiy...
18/09/2025

Muli ndi kuthekera kokudya zakudya zakasinthasintha? Musanyalanyaze kuchita motero. Zindikirani kuti zakudya zosiyanasiyana zimakhalanso ndi zopatsa thanzi (nutrients) komanso michere yosiyanasiyana.

Nthawi zina nsima izipuma ngati kuthekera kulipo!
!

DIABETESA condition where blood sugar levels are higher than normal.Type 1 Diabetes: When the pancreas is unable to prod...
20/08/2025

DIABETES
A condition where blood sugar levels are higher than normal.

Type 1 Diabetes: When the pancreas is unable to produce enough insulin which facilitates glucose uptake by the body.

Type 2 Diabetes: When the body is failing to respond to insulin being produced

Type 2 Diabetes is the most common and mostly affects adults.

SYMPTOMS
_Increased thirst, slow healing wounds, fatigue, blurred vision, weight loss, frequent urination, frequent skin/vaginal yeast infections.

CAUSES
_Hormonal imbalance, genetic mutations, pancreatic damage, and insulin resistance.

COMPLICATIONS
_Diabetes-related ketoacidosis, heart disease, stroke, kidney problems

PREVENTION
_Physical exercise, healthy diet, manage stress, adquate sleep, quit smoking.

Visit the hospital for sugar monitoring!

Exclusive breastfeeding (6 months)Breast milk doesn't only provide energy for the baby, it is rich in nutrients essentia...
30/07/2025

Exclusive breastfeeding (6 months)

Breast milk doesn't only provide energy for the baby, it is rich in nutrients essential for the growth and development of the baby. It also contains maternal (natural) antibodies that help to fight against infections.
Exclusive breastfeeding should start an hour after delivery up to six months.

13/07/2025

Komabe kumaziteteza, moyo ndi kamodzi! 🚢🚢🚢

Kuthamanga kwa magazi (Hypertension)Iyi ndi nthenda yomwe ikuononga achinyamata ambiiri m'chibisira!Zina mwa zomwe zikut...
07/07/2025

Kuthamanga kwa magazi (Hypertension)

Iyi ndi nthenda yomwe ikuononga achinyamata ambiiri m'chibisira!

Zina mwa zomwe zikutiika ife achinyamata pa chiopsezo cha matendawa ndi monga:
1. Kusuta fodya
2. kudya zakudya za nchere wambiri
3. kukhala osachita masewero olimbitsa thupi
4. kudya zakudya za mafuta ochuluka maka oundana
5. kumwa mowa

Kuthamanga kwamagazi kumaika ziwalo zina monga mtima pa chiopsezo.
Dziwani mlingo wa kaendedwe ka magazi mthupi mwanu pokalingisa ku chipatala (BP check)

_Mutu ukupweteka?_Maso alowa nkati?_Mukunva kutopa?_Nkodzo ukutuluka ochepa?_Nkamwa, milomo, kapena lilime zauma?_Nkodzo...
03/07/2025

_Mutu ukupweteka?
_Maso alowa nkati?
_Mukunva kutopa?
_Nkodzo ukutuluka ochepa?
_Nkamwa, milomo, kapena lilime zauma?
_Nkodzo ukutuluka wa chikasi komanso wa fungo?
_Mukunva luzu?

Izi ndi zina mwa zizindikiro za kusowa kwa madzi mthupi. irrigate our bodies with clean and safe waterπŸ’§πŸ΅

The magic behind Garlic (Allium sativum)πŸ§…1. Improves the immune system2. Has anti- cancer properties3. Has anti-viral, a...
01/07/2025

The magic behind Garlic (Allium sativum)πŸ§…

1. Improves the immune system
2. Has anti- cancer properties
3. Has anti-viral, anti-bacterial properties
4. Reduces cholesterol levels hence reducing the risk of cardiovascular diseases
5. Prevents intestinal diseases
6. Has ani-diabetic properties
7. Helps in the treatment of acute respiratory infections and influenza.

29/06/2025

Scurvy!

BEANS!Katundu womangira thupi uyu... it arrests the bodyπŸ˜‚πŸ€£these seeds are rich in proteins.
29/05/2025

BEANS!
Katundu womangira thupi uyu... it arrests the bodyπŸ˜‚πŸ€£

these seeds are rich in proteins.

29/05/2025

Aile

Iwe mdula moyo Edzi!!!......kwinako malizani nokha... Ndakatulo izi ndi za akuluakulu osat ana amma 2000!πŸ˜…πŸƒβ€β™‚οΈπŸƒβ€β™‚οΈπŸ™Œ
13/05/2025

Iwe mdula moyo Edzi!!!......

kwinako malizani nokha... Ndakatulo izi ndi za akuluakulu osat ana amma 2000!πŸ˜…πŸƒβ€β™‚οΈπŸƒβ€β™‚οΈπŸ™Œ

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The health Hub posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram