Moyo Wa Thanzi Kwa Onse

Moyo Wa Thanzi Kwa Onse Timathandiza anthu kuti achile ku matenda osiyanasiyana.

Why Wait When You Can Act Now with Rocenta? • Don’t let high BP progress into a stroke. • Avoid diabetes complications l...
30/07/2025

Why Wait When You Can Act Now with Rocenta?
• Don’t let high BP progress into a stroke.
• Avoid diabetes complications like leg amputation.
• Protect your vital organs from an enlarged prostate.
• Ensure wounds on your legs heal effectively.
• Safeguard your vision before it’s too late.
• Address fibroids early, before they grow larger.

Rocenta Stem Cell Therapy is a revolutionary solution that targets over 130 known diseases naturally and effectively.

Don’t delay your health journey—choose Rocenta today and experience the difference!

Take charge of your health now! ✅

Rocenta is now at k127,000 per box.
Minimum dosage is two boxes.

We have a shop in Blantyre but we also send everywhere.
Contact our consultant on 0999420917

*KUTHANA NDI MAUKA (VAGINAL YEAST INFECTION)* Mauka amatha kugwiri aliyese. Mayi kapena bambo. Mwana komaso wamkulu.Mauk...
19/07/2025

*KUTHANA NDI MAUKA (VAGINAL YEAST INFECTION)*

Mauka amatha kugwiri aliyese. Mayi kapena bambo. Mwana komaso wamkulu.

Mauka Ali mgulu la matenda opatsirana pogonana komaso zimatheka kwa azimayi ndi ana kukhala nawo munjira yosati yogonana.

Matendawa amayamba chifukwa Cha tizilombo tina tomwe timapezeka ku ndata mwachilengedwe. Ngati mzimayi chisamaliro chikhala chocheperapo, tizilomboti timatha kuchulukana ndikuyamba Matenda a mauka.

Ana amatha kuwatenga ngati agwiritsa ntchito ziwiya zosambira zomwe munthu yemwe Ali nd mauka agwiritsa nawoso ntchito. Koma izi sizichitika chitika.

Abambo amatenga matendawa munjira yogonana basi.

ZINA MWA ZIZINDIKIRO ZA MAUKA

AMAYI

1. Kuyabwa kundata
2. Kumva kupweteka pokodza
3. Chikazi choyera chopanda fungo (white va**nal discharge)
4. Kumva kupweteka pogonana

5. Kufiiraso pamwamba pa ndata

Zizindikiro zimenezi zimachulukira ukamayandikira period

ABAMBO

Azibambo ambiri amamvanso kukokana kwa mitsempha,

Amatulukaso matuza (sungu) kutsogolo kwa p***s plus kuyabwa

KUPEWA MAUKA
1. Avoid washing your va**na with soap
2. Avoid washing your va**na ndi madzi otentha
3. Keep your va**na dry nthawi zonse
4. Mupewe kuvala zinthu zothina kwambiri nthawi yayitali.
5. Mukamagona, musamavale panti. Pezani zovala zina zovala pogona koma zoti muzipitidwa mphepo.
6. Muzivala ma pant ouma komanso oyera. Change pants frequently.
7. Always put a small piece of cloth inside of your va**na to help keep it dry and tight.
8. Avoid kumangomwa ma antibiotics palipose. Muzimwa pokhapokha ngati simungathe kupilira
9. After using the bathroom , wipe from front to back avoid spreading yeast or bacteria between your a**s, urinary tract, or va**na.

Mankwala a mauka tili nawo,box imodzi k120,000, standard dosage two boxes.

Tiyankhuleni pa 0999420917

*Finally Yankho lanu lafika ndi a Dynace* . Iwotu adza ndi ma products ( Dynace Rocenta and Acebrew Cofee) omwe akuthand...
18/07/2025

*Finally Yankho lanu lafika ndi a Dynace* . Iwotu adza ndi ma products ( Dynace Rocenta and Acebrew Cofee) omwe akuthandiza ku mavuto osiyanasiyana a mnthupi (nthenda iliyonse). Monga kuthamanga kwa magazi (BP), mavuto amafupa, mavuto a masana ndi ma joints, mavuto a sugar ( Diabetes), Mavuto aubereki, kuonjezera mphamvu mnthupi , mavuto a maso, kuonjezera chitetezo mnthupi,mwina muvutika ndi menopause azimai thandizo lilipo ndithu, amathandizaso ku matenda osiyanasiyana amgonagona.

komanso ngati kuti mufuna kuonda chifukwa mwanenepesa hehehe musataye nthawi yambani kugwilitsa ntchito Dynace urbanism ( sliming candy)ndipo muzasimba lokoma.

Palinso Mwai kwa omwe angakonde kukhala ma distributor. Gulani any product pompo pompo ndekuti mudzapangidwa Signup.

Omwe afuna kumva Zambiri, tiyankhuleni pa number ili munsimu. Ngati muli kutali osadandaula timatumiza Kulikonse. moyo ndi mpamba, uchengetereni

*MAJOR HEALTH BENEFITS OF DYNACE PRODUCTS*

1. Powerful antioxidant to delay the progress of aging, promote cell regeneration, rejuvenation, repairs etc.

2. Enhance the immune system

3. Eliminates the environmentally polluted substance and heavy metals from the body

4. Promote the slimming effect

5. Improve sleep quality

6. Boost metabolism

7. Improve circulation

8. Reduce the risk of the metabolic disorder symptoms

9. Regulates blood sugar level

10. Repair DNA

11. Sharpen your memory, and cognitive function

12. Improve eyesight and vision

13. Support joint and bone health

14. Boost energy

15. Enhance nutrient absorption in the body

Tiyankhulane pa +265999420917

Anzanu ayamba kale kuchira muchedweranji?

Promotion prices ndi k120,000 pa box imodzi iliyonse, until further notice.

We have a shop in Blantyre but we also send everywhere your cost.

04/06/2025

Stress may kill your dreams.

Delete negative thoughts

Different worlds, one bond.He lived in the depths, calm and thoughtful.She soared in the skies, free and full of life.Un...
03/06/2025

Different worlds, one bond.
He lived in the depths, calm and thoughtful.
She soared in the skies, free and full of life.

Until someone questioned it:
Why waste your time with a fish?

She didn’t defend him. She let doubt creep in.
And she flew away… waiting for him to prove his worth.

He did. Against tides, predators, and exhaustion, he came. But she never showed up.
And one day… he stopped coming.

When she finally returned, it was too late.
He had given everything for a friend who stayed silent.

And she learned:
📌True friendship isn’t about similarity.
📌It’s not distance that destroys, it's doubt.
📌When we fail to value what’s different, we lose something irreplaceable.

💬 True friendship is an act of love that transcends differences.
💬 The heart always finds a way to connect.

03/06/2025

Drinking water at least two litters per day for an adult results into great metabolism, good skin and increased immunity, reduced stress

Anyezi wofiira ndi wofunika kwambiri my thanzi Lanu, Zambiri tikamba
03/06/2025

Anyezi wofiira ndi wofunika kwambiri my thanzi Lanu, Zambiri tikamba

You can join us on WhatsApp group
03/06/2025

You can join us on WhatsApp group

WhatsApp Group Invite

03/06/2025

Every morning, after working up,you should pray, drink warm water,eat a fruit,and meditate.

*THE MOST POWERFUL PRODUCT YET PEOPLE DON'T KNOW**Unlock the Power of Dynace Ace Guard: 11 Amazing Functions! 🔓*Hey Dyna...
03/06/2025

*THE MOST POWERFUL PRODUCT YET PEOPLE DON'T KNOW*

*Unlock the Power of Dynace Ace Guard: 11 Amazing Functions! 🔓*

Hey Dynace Global rockstars! 🤩 Are you ready to discover the incredible benefits of our flagship product, Dynace Ace Guard? 🤔

This powerhouse supplement is packed with 11 amazing functions that can transform your overall health and wellbeing 🌈. Let's dive in and explore each of these incredible benefits! 🎉

*1. Strong Immune Booster 🧦*
Dynace Ace Guard helps to fortify your immune system, protecting you from illnesses and infections 🤧.

*2. Control and Balance Sugar Levels 🍮*
This amazing supplement helps to regulate your blood sugar levels, reducing the risk of developing insulin resistance and type 2 diabetes 🌟.

*3. Strong Antioxidant 🌿*
Dynace Ace Guard is rich in antioxidants, which help to neutralize free radicals and protect your cells from oxidative stress 🌸.

*4. Reduces Inflammation 🔥*
This incredible supplement has potent anti-inflammatory properties, which help to reduce inflammation and alleviate symptoms associated with chronic diseases 🌈.

*5. Enhances Quality Sleep 😴*
Dynace Ace Guard helps to promote deep, restful sleep, essential for physical and mental rejuvenation 🌙.

*6. Anti-Aging 🕰️*
This amazing supplement contains powerful anti-aging compounds that help to reduce fine lines, wrinkles, and age spots, promoting a more youthful appearance 🌸.

*7. Cell Repair 🔧*
Dynace Ace Guard helps to repair damaged cells, promoting healthy cell growth and regeneration 🌱.

*8. Cell Rejuvenation 🌈*
This incredible supplement helps to rejuvenate cells, restoring their natural function and promoting overall health and wellbeing 🌸.

*9. Cell Replacement 🔁*
Dynace Ace Guard helps to replace damaged or dying cells with healthy, new ones, promoting tissue repair and regeneration 🌱.

*10. Cell Regeneration 🔄*
This amazing supplement helps to regenerate cells, promoting healthy tissue growth and repair 🌈.

*11. Cell Reactivation

Protect Your Kidneys Naturally! 🌿💚- Reduces inflammation & oxidative stress 🔥- Improves kidney function & blood flow 💪- ...
30/05/2025

Protect Your Kidneys Naturally! 🌿💚

- Reduces inflammation & oxidative stress 🔥
- Improves kidney function & blood flow 💪
- Supports waste removal & overall well-being 🌟

All-Natural Ingredients:

✦ Bulgarian Rose Placenta
✦ Ashwagandha
✦ Bitter Melon
✦ Brown Sea W**d
✦ NMN & More

Try Rocenta Today! 🌟

Don't wait - protect your kidneys naturally! 💚

Order now & support kidney health! 💊
Rocenta is at k105,000 per box.
Minimum dosage is two boxes.
Whatsapp/Calls:+265999420917

*KODI MUKUDZIWA?* MALINGA NDI MMENE ANAPANGIDWIRA STC30,UKAYAMBA KUMWA,AMAKATHANA NDI MATENDA OSIYANASIYANA MTHUPI.Stc30...
29/05/2025

*KODI MUKUDZIWA?*

MALINGA NDI MMENE ANAPANGIDWIRA STC30,UKAYAMBA KUMWA,AMAKATHANA NDI MATENDA OSIYANASIYANA MTHUPI.

Stc30,amakachita detect mavuto amene ali mthupi, zikatero amakagawikana,nkupita komwe kuli Mavuto, dziwani kuti ngati muli ndi vuto la BP ndi ma ASADZI, stc30 AMAKATHANA ndi zonse,Kaya muli ndi vuto mchibelekero komanso shuga, stc30 AMAKATHANA ndi zonse.

Chabe kuti ngati mavuto achuluka,ma BOX oti mumwe amachulukanso,nde timakuuzani.

M***a kuona kuti maumboni timalandira daily,a matenda osiyanasiyana.

Stc30 amakhala mu ma box, ndipo box imodzi Muli ma sachet 15.

One box is now at k109,900.
MUKAGULA, Timapeleka upangiri wa kamwedwe.

Matenda monga miyendo,ma asadzi,mapazi,gas,bp yongoyamba kumene,ma BOX awiri amachira munthu.

Koma matenda okhalitsa, aaakulu,ma box timakuuzani kuchuluka kwake.

Ife a kampani ya Seperlife tili ndi office komanso Shop ku Blantyre.

Timatumizanso kulikonse kumene muli.

Yankhulani ndi special consultant wathu pa 0999420917 kuti akuthandizeni.

Address

Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Moyo Wa Thanzi Kwa Onse posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Moyo Wa Thanzi Kwa Onse:

Share