18/05/2025
*Nthenda ya chifuwa chachikulu ( tuberculosis )*
*Zizindikiro za nthenda ya chifuwa chachikulu*
Kukhosomola magazi komamso chifuwa chosatha .
Kutetha kwa nthupi ( fever ) komanso kuzizidwa .
Kupweteka pa chifuwa .
Kutuluka thukuta usiku .
Kutsika kwa malemeledwe a nthupi ( weight loss ) .
Kuthawa kwa chilakolako cha chakudya.
Kumva kutopa .
Kusasa mau
*Zoyambitsa nthenda ya chifuwa chachikulu*
Chizolowezi chokonda kumwa mowa .
Kusuta fodya .
Mankhwala akuchipatala oletsa kukhosomola pamene munthu wadwala chifuwa .
Tizilombo toyambitsa matenda tama bacteria totchedwa mycobacterium tuberculosis .
Kuchepa kwa madzi nthupi.
Nthenda ya sugar .
Kukonda zakudya za nyama , mkaka , mazira Ndi nsomba komanso Kukonda kudya zakudya zokonola .
Ma soft drinks Ndi zakudya zina za sugar kwambiri
*Kuchiza nthenda ya chifuwa chachikulu*
Kondani kudya zakudya zokhala Ndi vitamin C ngati malalanje , mandimu manyumwa , bwemba , malambe , nanazi apozi ndikumwa ma juice ake ,
Pangani juice wa anyezi Kapena garlic amatsuka njira ya mapapo , akwane 250 mls ,
Ukamirani madzi otetha mutaikamo mpungabwi kapena masamba a bluegum a bwinobwino ,
Imwani tiyi wa mint amatsekula njira zamapapo , wiritsani madzi paokha ndikuthira masamba a mint , imwani madzi okwana 250 mls , pangani izi katatu patsiku ,
Imwani tiyi wa black pepper powder amapha tizilomboti , tengani half teaspoon mu madzi okwana 250 mls , pangani izi katatu patsiku ,
Tiyi wa green tea amathandizaso , tengani half teaspoon mu madzi okwana 250 mls otetha ,
Tiyi wa masamba a pine kapena khungudza , kuwiritsa dzanja limodzi mumadzi okwana lita limodzi kwa 10 minutes, imwani 300 mls mamawa ndi 300 mls masana ndi 300 mls madzulo ,
Imwani tiyi wa lemon grass okwana 250 mls ,
Pangani juice wa nthochi kuti m***ane ndi mvuto lakutopa ,
Wiritsani ginger , garlic Ndi kudula mandimu mapisi ang'ono ang'ono kuponya momwemo sefani madzi akewo ndikusakaniza Ndi uchi imwani tsiku lonse koma madzi akhale okwana lita limodzi ,
Idyani mtedza wa walnuts , mafuta opezeka mu mtedzawu amachotsa kutupa ,
Imwani tiyi wa turmeric , wiritsani turmeric wa fresh dzanja limodzi mutamusinja mu madzi okwana lita limodzi , mumwe mamawa 300 mls , masana 300 mls , madzuloso 300 mls ,
Cayenne pepper kutenga quarter teaspoon kuthira mu madzi otetha okwana 150 mls Ndikumwa , pangani izi katatu patsiku ,
Salani kudya masiku atatu ndikudya zipatso zokhazokha kapena ma salads pa mwenzi ulionse ,
Kondani kumwa madzi okwanira maka otetha mamawa ,
Khalani malo omwe pali mitengo yambiri , komanso m***a kupita malo omwe kuli mtsinje wothamanga kunakhala mpweya wabwino ,
Pangani masewera olimbitsa nthupi tsiku ndi tsiku .