Lumbira Health Centre

Lumbira Health Centre We have well qualified technocrats and good supporting staff who will help you when you visit our fac

22/12/2024
22/12/2024

Bwerani ku Chipatala chanu cha Lumbira ku Mitsidi kuti muzapeze thandizo la Chipatala mwachangu

24/08/2024

Hello . Lumbira/Mitsidi Health Centre mogwirizana ndi Blantyre DHO ikulengeza za kusamutsidwa kwa ntchito za uchembere wabwino kuchoka ku Chilomoni kupita ku Lumbira/Mitsidi. Izi zichitika kuyambira pa 26 August 2024 kufikira mtsogolo muno.

Izi zili chomwechi chifukwa mu nthawi imeneyi Blantyre DHO ikhala ikukonza chipinda chomwe amayi oyembekezera amachiliramo.

Choncho amayi onse oyembekezera òmwe amachilira ku Chilomo akupemphedwa kulunjika ku Lumbira/Mitsidi komwe akathandizidwe moyenera.

Zikomo.

27/05/2024

, we welcome all our new members to this page.

Address

Sigerege Sanjika Road
Chilomoni

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Lumbira Health Centre posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram