Frank Wa Zachilengedwe

Frank Wa Zachilengedwe Ngati mwamva nthupi choyamba pitani kuchipatala akapeze vuto kenako bweran muzapeze thandizo
0️⃣9️⃣9️⃣2️⃣4️⃣4️⃣9️⃣4️⃣4️⃣2️⃣➕0️⃣8️⃣8️⃣4️⃣5️⃣6️⃣4️⃣2️⃣1️⃣3️⃣

MALAMBE.CHECK COMMENT BOX AND FOLLOW Frank Wa Zachilengedwe           👇👇👇👇👇👇👇
20/04/2026

MALAMBE.

CHECK COMMENT BOX AND FOLLOW Frank Wa Zachilengedwe


👇👇👇👇👇👇👇

Munthu emwe wakhala akudwala nthawi yaitali kwazaka zaka kumwa mankhwala koma ataa osagwila ntchito mukatchole masamba a...
20/04/2026

Munthu emwe wakhala akudwala nthawi yaitali kwazaka zaka kumwa mankhwala koma ataa osagwila ntchito mukatchole masamba anthochi owuma akakhale okwanila ndithu mukatero mukawaika muchimpoto chachikulu ndi madzi okwanila akawire mokwanila ndithu .akawira azizile poti munthu ndikusamba .mumusambise munthu uja pogwiritsa ntchito zimasamba zija ngat siponje kuyambira kumutu mpakana kumapazi thupi lonse

Madzi enao mumumwese odwala uja pasiku kawiri half cup kwamasiku atatu mukatero muyambirenso kumupasa munthu uja mankhwala akuchipatala ake aja amayamba kugwira ntchito nthupi within 7 days munthu ameneyo achila kaya

Kaya ndinuo achibale anu ndaibweresa chifukwa ambiri post imeneyi yawapindulira umboni wina watipeza

Anthu omwe mavutisidwa ndi afiti kudandaula maloto komanso kutambilidwa kosatha timatenga masamba owuma anthochi ndikuika kumutu tsiku limenelo muzagona tulo ngati mwana .alendo naonso athandizike nao

20/04/2026

KWACHA TSOPANO

UBWINO WA RED JATROPHA.Check comment section and follow Frank Wa Zachilengedwe       👇👇👇👇👇👇
19/04/2026

UBWINO WA RED JATROPHA.

Check comment section and follow Frank Wa Zachilengedwe

👇👇👇👇👇👇

19/04/2026

TIYENI KU CHURCH

KUTHANA NDI ZIKANGA.Check Comment Section and follow Frank Wa Zachilengedwe       👇👇👇👇👇👇
18/04/2026

KUTHANA NDI ZIKANGA.

Check Comment Section and follow Frank Wa Zachilengedwe


👇👇👇👇👇👇

RED JATROPHA follow Frank Wa Zachilengedwe      ゚viralシfypシ゚viralシalシ
18/04/2026

RED JATROPHA

follow Frank Wa Zachilengedwe
゚viralシfypシ゚viralシalシ

Lero ndangot Gululu ndi ma Full Chicken ang'ono ang'ono 😂😂😂😂Kalibu.Follow Frank Wa Zachilengedwe      ゚viralシfypシ゚viralシ...
18/04/2026

Lero ndangot Gululu ndi ma Full Chicken ang'ono ang'ono
😂😂😂😂
Kalibu.

Follow Frank Wa Zachilengedwe

゚viralシfypシ゚viralシalシ

18/04/2026

_*🙏📖MAU A LERO📖🙏*_
_Ahebri 11:6 koma wopanda cikhulupiriro sikutheka kumkondweretsa; pakuti iye wakudza kwa MULUNGU ayenera kukhulupirira kuti alipo, ndi kuti ali wobwezera mphotho iwo akumfuna iye._

Popemphera, tiyenera kukhala ndi chikhulupiriro chonse kuti MULUNGU akumva. MULUNGU sakondwera ndi anthu amene akamaliza kupemphera amayamba kukaikira kuti, “Kodi wandimvadi kapena ayi?” Tiyeni timusangalatse MULUNGU ndi chikhulupiriro cholimba, chifukwa amayankha mapemphero athu molingana ndi chikhulupiriro chimene tili nacho. AMEN
*HAPPY SABBATH*

UBWINO WA GARLIC.  Remedy Check ku Comment Section and follow Frank Wa Zachilengedwe      ゚viralシfypシ゚viralシalシ   👇👇👇👇👇👇...
17/04/2026

UBWINO WA GARLIC.
Remedy Check ku Comment Section and follow Frank Wa Zachilengedwe

゚viralシfypシ゚viralシalシ
👇👇👇👇👇👇👇

UBWINO WA MBATATA YA KHOLOWA.Check Comment Box and Follow Frank Wa Zachilengedwe      ゚viralシfypシ゚viralシalシ 👇👇👇👇👇
17/04/2026

UBWINO WA MBATATA YA KHOLOWA.

Check Comment Box and Follow Frank Wa Zachilengedwe

゚viralシfypシ゚viralシalシ
👇👇👇👇👇

REMEDY YA MENE TINGASUKIRE ZIWALO ZA NTHUPI IZI.Follow Frank Wa Zachilengedwe 1. KUSUKA CHIWINDI 2. KUSUKA IMPSYO 3. THA...
16/04/2026

REMEDY YA MENE TINGASUKIRE ZIWALO ZA NTHUPI IZI.
Follow Frank Wa Zachilengedwe

1. KUSUKA CHIWINDI
2. KUSUKA IMPSYO
3. THANZI LA MTIMA
4. KAGAYIDWE KA CHAKUDYA

video yokhudza izi taponya kale.
Link ili mu comment Box

゚viralシfypシ゚viralシalシ

Address

Nangula
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Frank Wa Zachilengedwe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share