23/12/2025
*LIKANGO/HEMORRHOIDS/PILE/MUDZI*
0994627648
✅Takhala tikumva nkhani yokhuza likango kwa nthawi yaitali ndipo ambiri mwa ife sitidziwa kuti kodi likango ndi chani nanga limakhala motani
Kukamba mwachidule akati likango ndiko kutupa kwa misempha yapa re**um
*MAGULU A LIKANGO*
👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽
Likango lili mmagulu awiri monga
😩LIKANGO LA MKATI
😩LIKANGO LOTULUKA
*ZOMWE ZIMAYAMBISA LIKANGO*
1,Kusowa kwa iron nthupi
2,Kunyamula zolemela
3,Kuzimbidwa kwa serious.
4,Kugonana pogwilisa njira ya kumbuyo.
5,Azimayi nthawi yobeleka pomwe amayesela kukankha paja (ngakhale from 6 months mwachidule mimba imatha kuyambisa likango kwa ena).
6,Low fiber diet
7,Obesity
8,Kugonedwa ndi anthu omwe adanyanyalilidwa gadafi (Zipangizo zazikulu zikulu)
9,Colon cancer
10,Kutsekula mmimba
11,Rectal surgery.
12,Bowel disorder kungokambapo zochepa
*ZIZINDIKIRO ZOTI MULI NDI LIKANGO* 👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽
M***a kudziwa kuti muli ndi Likango poona zidzindikiro izi
Kutuluka chinthu kobibila chomwenso chimatha kutuluka magazi ndipo chimapweteka.
Mukamaliza kubiba mkumamvabe ngati simudabibebe.
Kuyabwa kobibila.
Pena kutulusa chimbuzi chosakanikilana ndi zimamina.
Kumva kuwawa pobiba ndi zina zomwe sindidakwanisepo kuzilemba.
*KUYIPA MWA LIKANGO* 👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽👇🏽
1,Kubeleka mwana kumwalira
2,Umuna kumatuluka after ej*******on
3,Kupangisa Mkazi kusabeleka
4,Kubeleka mwana kukula pang'ono kumwalira
5,Likango lokupha amuna