Kambe Herbal Healthcare Clinic

Kambe Herbal Healthcare Clinic Hope for the pioo to stay health and strong living

13/10/2024

*Kambe Herbal Healthcare Clinic*

+265 888 394 309

*What is a CD4 count?*

✍🏾 A CD4 count is a blood test to check the amount of CD4 cells in the body. CD4 cells are a type of white blood cell. They play a key role in the immune system. They alert other immune cells to the presence of infections such as bacteria and other viruses in the body.

πŸ‘‚πŸΌ When a person is living with HIV, the virus attacks the CD4 cells in their blood. This process damages CD4 cells and causes the number of them in the body to drop, making it difficult to fight infections and the body's natural defense weakens sognificantly.

πŸ‘‚πŸΌ CD4 counts show the strength of the immune system. A healthy immune system normally has a CD4 count ranging from 500 to 1,600 cells per cubic millimeter of blood. When a CD4 count is lower than 200 cells per cubic millimeter, a person will receive a diagnosis of *AIDS.*

*Kambe Herbal Healthcare Clinic*
+265888394309

_hope for the pipo to stay health and strong living always_

13/10/2024

*Kambe Herbal Healthcare Clinic*

+265 888 394 309

*URINARY TRACT INFECTION (UTI) --MATENDA A NCHIKODZODZO*

✍🏾 Sometimes you feel pain when urinating,mikodzo kusintha mtundu komanso nthawi zina kuwawa mmimba cha pansi pa nchombopa and you wonder what it is!This in some cases is Urinary Tract Infection (UTI).

πŸ‘‚πŸΌ Bvutoli limabwera pamene tizilombo ta bacteria talowa mu chikodzodzo (bladder --Cystitis) kapena njira ya mkodzo (urethra--Urethritis) nkuyambisa timabala or tizilonda mkatimo tomwe timapangisa zizindikiro zimenezi.Nthawi zina when the condition is serious infection imeneyi imatha kufikanso mma kidney (pylenonephritis).

πŸ‘οΈ Zizindikiro zina zoti munthu uli ndi UTI ndi monga kumva kuotcha pokodza,kukodza nkodzo osakanizana ndi blood kapena ooneka cloudy,black (like cocacola),kukodza pafupipafupi koma pang'ono,strong smelly urine.

πŸ‘‚πŸΌ Urinary tract infection is common in women chifukwa cha chilengedwe chawo makamaka chifukwa amakhala ndi urethra (njira ya kodzo) ndi yaifupi komanso pafupi ndi njira ya chimbudzi komanso nthawi imene mayi wakula kukhala ku menopause kuchepa kwa ma hormones ena monga estrogen kumapangisa va**nal dryness komanso kukhala pachiopsezo chopanga UTI.

*Note*
πŸ‘‰πŸ½ Ndibwinonso kuzindikira kuti matenda opatsilana ena amatha kubwera ndi zizindikiro zonga zomwezi kuphatikizapo kupanga nkodzo wosakanikirana ndi mafinya komanso kuwawa pokodza modabwitsa.Mukapita kuchipatala amadziwa kusiyanitsa zinthu zimenezi.

By
Kambe Herbal Healthcare Clinic
+265 888 394 309

_hope for the pipo to stay health and strong living always_

13/10/2024

*Kambe Herbal Healthcare Clinic*

+265 888 394 309

*ULCERS*

*NGAT MUKUVA IZI THUPI MWANU*

1. KUOTCHA PA CHIFUWA (CHEST BURN)

2. MSERU

3. KUSAZA

4. PASING EXCESSIVE AMOUNT OF GAS
( KUPHWISA PHWISA PAFUPI PAFUPI)

5. KUPWETEKA PACHIFUWA

6. KUPWETEKA PAMWAMBA PA MIMBA

7. KUOTCHA PAMWAMBA PA MIMBA

8. KUPWETEKA KWA M'MIMBA

9. FEELING OF FULLNESS

10. FEELING UNCOMFORTABLY AFTER EATING

11. KUZIVA OKHUTA

12. KUPANGA CHIMBUZI CHAKUDA KAPENA CHOONEKA NGAT MAGAZI MAGAZ CHOCHO

13. KUPWETEKA KWA M'MIMBA MUKADYA ZOLIMBA KWAMBILI

*_Tangoyambani Kambe Herbal Green Detox Powder or Juice._*

By
kambeherbajuice@gmail.com
+265 888 394 309.

_hope for the pipo to stay health and strong living always_

13/10/2024

Kambe Herbal Healthcare Clinic
Calls Or Whatsap
πŸ‘‡
+265 888 394 309

MAUKA (VAGINAL YEAST INFECTION)

πŸ•ΈοΈ Mauka amatha kugwiri aliyese. Mayi kapena bambo. Mwana komaso wamkulu.

πŸͺ Mauka Ali mgulu la matenda opatsirana pogonana komaso zimatheka kwa azimayi ndi ana kukhala nawo munjira yosati yogonana.

πŸ‘‰πŸ½ Matendawa amayamba chifukwa Cha tizilombo tina tomwe timapezeka ku ndata mwachilengedwe. Ngati mzimayi chisamaliro chikhala chocheperapo, tizilomboti timatha kuchulukana ndikuyamba Matenda a mauka.

πŸ‘‰πŸ½ Ana amatha kuwatenga ngati agwiritsa ntchito ziwiya zosambira zomwe munthu yemwe Ali nd mauka agwiritsa nawoso ntchito. Koma izi sizichitika chitika.

πŸ‘‰πŸ½ Abambo amatenga matendawa munjira yogonana basi.

*ZIZINDIKIRO ZA MAUKA*

*AMAYI*

1. Kuyabwa kundata
2. Kumva kupweteka pokodza
3. Chikazi choyera chopanda fungo (white va**nal discharge)
4. Kumva kupweteka pogonana

5. Kufiiraso pamwamba pa ndata

_Zizindikiro zimenezi zimachulukira ukamayandikira period_

ABAMBO

πŸ•ΈοΈ Azibambo ambiri amamvanso kukokana kwa mitsempha,

πŸ‘‰πŸ½ Amatulukaso matuza (sungu) kutsogolo kwa p***s plus kuyabwa

KUPEWA MAUKA

1. Avoid washing your va**na with soap
2. Avoid washing your va**na ndi madzi otentha
3. Keep your va**na dry nthawi zonse
4. Mupewe kuvala zinthu zothina kwambiri nthawi yayitali.
5. Mukamagona, musamavale panti. Pezani zovala zina zovala pogona koma zoti muzipitidwa mphepo.
6. Muzivala ma pant ouma komanso oyera. Change pants frequently.
7. Always put a small piece of cloth inside of your va**na to help keep it dry and tight.
8. Avoid kumangomwa ma antibiotics palipose. Muzimwa pokhapokha ngati simungathe kupilira
9. After using the bathroom , wipe from front to back avoid spreading yeast or bacteria between your a**s, urinary tract, or va**na.

Tiphuzire zaukhondo chifukwa ndiudindo wa aliyese M'mayi or M'mbambo kudzisamalila

By
Kambe Herbal Healthcare Clinic
+265 888 394 309

11/06/2024

RIP VP

Kambe Herbal Healthcare Clinic ....umboni wa madala ku Area 38 ...Amadwala Stroke koma mwachisomo chamulungu zatheka ndi...
10/11/2023

Kambe Herbal Healthcare Clinic ....umboni wa madala ku Area 38 ...Amadwala Stroke koma mwachisomo chamulungu zatheka ndilimodzi ...Na**so Amene Mwamwa ma Herbal Enawo osachira No Worries Tangoimbani or Whatsap itanitsani wanu Kambe Herbal Detox Juice Remedy Na**so muzakhale mboni ndithu...+265 888 394 309

Timatumiza World Wide kulikose kunjakomwe Nsanje to Chitipa Available

Ma beach

Lilongwe

Machinga

Mulanje

Limbe

Stay blessed PAMENE mukupanga chiganizo chozayamba kumwa nawo Kambe Herbal Detox Juice Remedy ...mulungu akudalitseni

16/10/2023

*Kambe Herbal Healthcare Clinic*

+265 888 394 309

*ZAMAKHWALA ACHIZUNGU NDI ACHILENGEDWE*

▫️Mankhwala A Chizungu Amawapanga Kuchokera Ku Za Chilengedwe, M'meneso Aliri Kambe Herbal Detox Juice.

β–ͺ️ Tikayang'anitsitsa Zakale Mankhwala Oyambirira Munthu Akati Akamwa Amachiriratu. Ataona Kuti Sazipanga Ndalama, Mpamene Analinganiza Kuti Azisakanizamo Ma Chemicals.

πŸ‘‰πŸ½ Ngati M'mene Kambe Herbal Detox Juice Remedy Akuchizira Anthu Kenaka Basi Nkumaikamonso Ma Chemicals Oti Anthu Asamachiriretu.

β–ͺ️Ma Chemicals Omwe Amaikidwa M'mankhwala A Chizungu Ndiamene Akumaononga Chiwindi.

▫️Chiwindi Chikamafooka Ziwalo Monga Ma Kidneys, Kapamba, Ndulu, Thyroid Gland, Prostate, Mtima, Mapapo Ndi Zina Zimayamba Kufooka, Mwina Kumatupa, Kukhala Ndi Zotupa, Matuza Ndi Zina. Zikatere System Ya Thupi Lonse Limasokonekera Ndipo Munthuyo Amakhala Customer Wa Mphamvu Wa Pharmaceutical Companies. Nyambo Yake Ndi Zakumwa Ndi Zakudya Za Ma Chemicals Omwe Amachititsa Chiwindi Kusamagwira Bwino Ntchito.

By
Kambe Herbal Healthcare Clinic
+265 888 394 309

_Hope For The Pipo To Stay Health And strong Living Always_

Happy mother's day to u all mother's in this groupKambe Remedy promotion til Friday 1 litre 10,0005 litres 25,000 I wish...
16/10/2023

Happy mother's day to u all mother's in this group

Kambe Remedy promotion til Friday

1 litre 10,000
5 litres 25,000

I wish u a lovely holiday u all mother's

Call or Whatsap
+265 888 394 309

Nsanje to Chitipa ndikutumizaso malire Ndi friday

Address

Kambe Herbal Healthcare Clinic . . . P. O. Box 13, Champhira , Mzimba
Lilongwe

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Kambe Herbal Healthcare Clinic posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Kambe Herbal Healthcare Clinic:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram