Pabwalo sweet stories & Addvitisement

Pabwalo sweet stories & Addvitisement it's where you can have sweet stories and advertising what you have

Guys osamangoti ife ndife a kwaya timaimba , koma kwaya iyiyi yabwela kuzakhala.the so called   PASSOVER ngati simudawon...
21/03/2025

Guys osamangoti ife ndife a kwaya timaimba , koma kwaya iyiyi yabwela kuzakhala.the so called PASSOVER ngati simudawonele tangopitani ku koment section muli link muwone zomwe kwaya iyi ikuchita.

Do you know this guy? If you know Kodi mfundo zake mwazilandila bwanji? Tiuzeni maganizo anu ?
24/01/2025

Do you know this guy? If you know Kodi mfundo zake mwazilandila bwanji? Tiuzeni maganizo anu ?

Do you know what this guy ? Kodi mfundo zomwe amakamba Inu mmazimvesa bwanji?, Tiuzeni ndemanga yanu ?
24/01/2025

Do you know what this guy ? Kodi mfundo zomwe amakamba Inu mmazimvesa bwanji?, Tiuzeni ndemanga yanu ?

My Mother's heartShort story by James George mulengaDon't forget to like and follow this page for more storiesSceen 1Lov...
27/02/2024

My Mother's heart

Short story by James George mulenga

Don't forget to like and follow this page for more stories

Sceen 1

Love is blind

Ooooo nono no this is an fair!!! God why you allowed this to happen?

Joe my son pleas come and eat since morning you didn't eat anything what is bothering you ?

Joe ; mama it's getu mama she is dieng at the hospital ?
Mama:what happening to your fiance
Joe ; mama I told you that she had deficult with her heart,

Mama : am sory my son,don't wory she will be fine come and eat we save a miracle God she will be fine
Joe ; mama how can I eat while my heart is not feeling well ,yesterday the doctor said that she remain with 48 hours if there will be nobody to donate a heart to her I will lose her ,
Mama : ooo my son am sorry I didn't know that it reach to that mess eash

Joe ; mama ooo no if getu will die and I will die with her I don't want to lose her
Look mama what will I be if I lose her she is my happiness my everything oo no God have pity on me pleas.

Mama ; my son don't wory come and eat first I will go with you to the hospital oky I know what to do oky

My only son ,akufuna kudzipha chifukwa Cha msikanayu zoona kutheka amamukonda kwambiri no ndidamuvutikila mwanayu kuti abadwe akule ndye ndingomuluza mopheka chonchi no koma ndimupangile chinthu chomwe azanyadile moyo wake wonse akazamandikumbukila .

Tidanyamuka ine ndimwana wanga joe ulendo wakuchipatala ku central hospital.

Joe don't wory getu will not die ndipo ukamachoka kuno uzipita naye limodzi oky

Joe ; are you sure mamu ,I really trust you so mulch

Mdamuyangana mwana wanga kumwetulila kwake kudandukumbutsa nthawi imene atangobadwa kumene adamwetulila , ndidaziyankhulila ndekha ndukapeleka mtima wanga ngati msembe kuchimwemwe Cha mwana wanga ndi mpongozi wanga wa msigolo .

Ipitilile nkhaniyi Kodi kapena silibwino ma comment anu ndamene apangitse nkhaniyi kupitilila

∆∆∆∆∆∆∆∆∆ TRUE LOVER∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶A short story by James m...
26/01/2024

∆∆∆∆∆∆∆∆∆ TRUE LOVER∆∆∆∆∆∆∆
¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶∆∆∆∆∆∆∆¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶¶

A short story by James mulenga

Dont forget to like this page for more stories

Sceen 1

Mphuto yakalulu idakula mtazaoneni
...................................I love u so much
................................Box Ur my heart...................................Love is two pple

Dear my Love phwedo

Ndalemba kalatayi pofuna kukudziwitsa momwe ndikumvela,komanso kukudziwitsa chona chokhachoka maka pa chophweteka chomwe lelo lino dziko lidandikamo kuphatikizapo iweo .

Phwedo ineo sindine hule monga mmene dziko likuyankhulila komano zonsezi zidachitika chifukwa ndimakukonda kwambiri ndipo sindikafuna kukuluza.

My love mmene ukadwala muja nthenda ya ipsyo ija zimafunika ndalama yoti iweo upitile kuchipatala chakunja ndukalandila chithandizo komano palibe ndi mmodzi yemwe amaonetsa kuti andithandiza kuyambila abale ako komanso omwe umati ndi anzako apamtima onse amangoyangana mkumadikila infayako izitu zikandiphweteka siku ndi siku ndipo ndimakhetsa nazo misonzi mpaka mdayamba kusakasaka njila yoti ndipulumutsile moyo wako koma palibe chimathandiza kufikila pamene mdakumana ndi mponda matiki wina amene adandiuza kuti ndikagona naye andipasa ndalamazo .

Ndye popeza mdasowa mtengo wogwila ndidalolela kugona naye popeza Kwa ine padalibe chopambana kuposa moyo wako .

Pepani kuti ndinakubisila pokuza kuti ndalama yakuchipatala adandipatsa ndi ankolo anga ,komano zona zake mzokuti kwathunso ndife mphemvu mdyela ku mthiko palibe amene angapezeke ndi ndalama ngati imene ija.

Phwedo mkati mwanga mukuyaka moto ndikaona ngati ndibisa chinthu choipa ichi komano zidabwela pambalambanda chifukwa Cha mwana amene ndanyamulayu,pena ndimafuna nditangomwa mankhwala kuti ndikaphe kamwanaka koma ndidazizindikila kuti ndichiyembekezo chokhacho chomwe ndili nacho chomwenso chili chikumbutso changa pa chikondi changa pa iwe

Ndimakukonda phwedo kwambiri

Ndatha ine wachikondi wako Eliza

Kodi mudaesako kukwilila nthochi mu nthaka ? Nanga mutakwilila chidachitika ndichani ? Tapangani koment kapena like this...
05/01/2024

Kodi mudaesako kukwilila nthochi mu nthaka ? Nanga mutakwilila chidachitika ndichani ? Tapangani koment kapena like this page kuti mumve tsatanetsane wake!!!!

03/01/2024

KODI MWAYIMVA ?

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this page...
26/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️
A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 8

Ndidalowa mnyumbayi koma eee guys ndimaona ngati mwina ndafika dziko lina ,ndisaname chilichonse chimandipasa chidwi kuyangana mipando idali mnyumbayi sipamalephela kupezeka golide makapu eni eniwa nawonso adali agolide ndinganene table nayonso ndiyagolide ndinene kuti 80 % ya dzinthu zomwe zidali mnyumbayi zidali za golide ndidaziyankhulila ndekha is this a house or mparadiso?

Mwati; James wellcome to my house feel free
James; oo thanks
Mwati; glory grory?
Glory; maa am here
Mwati; Tenga chikwama ukasiye kuchipinda komwe azigona jameyi .
James umusatila glory kuti akakuonetse chipinda chako?
James;ooo thanks mwatitha
Mwati; your wellcome

Ndidauyamba ulendo wopita kuchipinda komwe ndikhale ndikugonako mopelekezedwa ndi ntsikana ameneyu glory

Glory;sir this is your room
James;ooo thanks koma sitidalonjelanetu ,moyo wabwino koma?
Glory;wabwino ndiope inu
James; wabwinonso ine dzina langa ndine James Banda iwe nanga?
Glory:monga udawamvela madam aja langa Zina ndine glory thengo ndine amene ndimasamalila nyumba ino

James;ooo nice to meet you
Glory;nice to have you in this house pakafunika chilichonse ndyekuti mundiuza.

Ndidalowa mchipinda mwangamu oo s**t Kodi mchipinda ichichi kapena nyumba ya payokha nanga chipinda mpakana kitchen,toilet mpakananso bathroom kkkk eee kuphunzila sikutha eti! Ngizizi tiona nazo zosaona ndithu ndidagona pa bedili mkumapumula.

Joe is this true ? Are you a such kind of guy ooo you killed me am deado!!; Osandiuza zoona zoti ur HIV positive?
Joe; love am sorry you know I love you so much sikuti sindimafuna kukuza komano kuti ndidali ndi mantha to tell you about my stutus
Love; oo no this not love udakakhala umandikonda zenizeni bwenzi utandiuzilatu koma wadikila tagonana gonana mosazitetezanso and mkudikilanso kuti ndifufunze ndekha no there is no love noonoo
Joe; baeb forgive me????

🇲🇼🇲🇼🇲🇼 THE BROKEN RING 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼A short story by James g mulengaDon't forget to like this pag...
25/12/2023

🇲🇼🇲🇼🇲🇼 THE BROKEN RING 🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼🇲🇼

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 1

Hey beautiful lady ,how are you?
Eeee you bitch don't touch me , don't even try to great me !!! Don't you see that I am a fiance to the next king of this Kingdom in fact I am the next queen of this Kingdom!!
Boy; so what's wrong in greating you?
Madam; kkkk you don't see where is wrong right can you come closer?

The boy goes closer to the girl and he was badly slapped

Boy ;madam you slapped me ?
Madam; yess I slapped you ,this will always reminded you that am not of your class and in addition that am not a ordinary girl whom you should call or touch without athorisation hope you head me clearly!!!
Boy: but madam what did I do to deserve this? But do you know who I am ?
Madam:kkkkk I don't need to know who you are !!! A peasant boy like a useless infact a reckless man like you may thunder hit you

I left the place but I was so disponted is this type of the girl my father chose for me to marry,no I can't marry that wicked girl.

Is this the way she will treat our people in this village? Thanks God for revealing this before I marry her eee I wana marry a monster

Let's meet mu next part coment or like this page for more stories happy xrimas I love you o

25/12/2023

Happy happy xrimas wishing everyone a wonderful Christmas I love you o

20/12/2023

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rhoda Mtenje Malikebu, Mayeso Afraid

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️ ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️A short story by James g mulengaDon't forget to like this pag...
18/12/2023

❤️❤️❤️ ITATHA MISONZI ❤️❤️❤️❤️❤️❤️ ❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️❤️

A short story by James g mulenga

Don't forget to like this page for more stories

Sceen 7

Kuyangana magalimoti amene adali ku mpandaku sindidasimikile kuti zinthu zotelezi zingapangidwe ndi munthu wa mkadzi

Mwati: jame bwanji ukungoti maso mwamwa ngati nkhuku yoti ifuna ikile madzila?

James: mwatitha ndisaname mutu wanga wasiya kugwila ntchito apapa magalimoti onsewa Ako?

Mwati:eya ndianga ndithu
James; BMw ,hummer mpaka six dors nduze chinsisi kapena mwina unajoina pansi pa njanja eti ?
Mwati: James sisataniki ayi izizi ndikugwila kwanga ntchito molimbikika kwandipangitsa kukhala ndi izizi ,ukamakhala uziziwanso kuti mulungu amadalitsa ndipo mau amulungu amati silver Gold zonse mzake za mulungu olo Iweo utamupempha akhonza kukupatsa

James; mwatitha zomene ulinazozi akukanika amuna kukhala nazo ndye Iweo munthu wamkazi zitheka bwanji? Ukundijamitsa malingalilo anga this is too much it's beyond my expectations I think there is something beyond this!!!.

Mwati; ukuganizatu molakwika James like area on ndidakufotokozela kuti akadzi osamawayanganila pansi nawonso Ali mkuthekela kopanga zazikulu nkhani mwanayo mulimbikitseni kaya ndi maphunzilo kaya busness ndimamva chisoni kwambiri makolo ena saerekeza olo kumulipilila mwana wa mkadzi sukulu ku secondary ati ayi azakwatiwa mamuna wake ndamene azizamusamala mchifukwa chake akazi ambiri akulandila nkhanza zosiyanasiyana mmabanja kamba koti amaziwa kuti banjalo likatha sangathe kuzimilila pa okha ndye amalolelabe kukhala mu ndende ya mabanja koma sichonchoyi aliyense angathe kuboleza

James: zoonadi sukulu sithadi pongokuonani inuo mwandisatsa phunzilo lalikulu komanso zomwe mwandiuzazo zandisegula malingalilo anga ndimawawona akadzi molakwika kwambiri apapa ndazindikila madam mwatitha mulungu salakwitsadi ngozi imeneyi yandipangitsa kuti ndiziwe zambiri
Mwati; kkkkk watelo tiye tilowe mnyumba

Jame;oky fine

Ndidalowa mnyumbayi guys eee koma ya ndimaona

Address

Lilongwe

Telephone

+265995994024

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pabwalo sweet stories & Addvitisement posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram