06/03/2026
Our Under-Five Clinic is currently underway at Waka pvt Clinic.
Parents and guardians are welcome to bring their children for growth monitoring, immunization, and health checks
Chipatala cha ana osakwana zaka zisanu chikuchitika pano pa facility yathu.
Makolo ndi osamalira ana akulandiridwa kubweretsa ana awo kuti adzalandire kuyezedwa kukula kwa thupi, katemera, ndi kuyezetsa thanzi