Fighting Against Hiv/Aids and Sti

Fighting Against Hiv/Aids and Sti ART AND STI CLINICAL MENTOR
(1)

03/09/2025

CONDOM IJAYI MUSAZAIPHWEKETSE. WINA APELEKELA UMBONI WA CONDOM UKU MISONZI IKUTCHUTCHA.

IWE PETULO IWE PETULO CHENJELA.

03/09/2025

Big shout out to my newest top fans! Annastatio H Glyn, Mike Kalambalika, Carolyn Mungomo, Grace Lopanda, Grace Macheso, Donnie Dunwell Nzima, Hannah Makweza, Leah Mtonga, Jessie Mbewe, Shadreck Shanto Kasimba, Elena CHilemba, Clems Makina, Annert Emmunuel, Gina Dinala Tembo, Friday Knight, Ajanto Kalen, Bridget Happy, Anold Kwenyengwe, Favoured Emil, Tau Nkhwazi, Charity Moyo, Promise Jonga, Robert WA Otchuka Limera, Gannho Mkakala, Alimando Kantchito, Kakato Master, Regie Lustica, Mecy Maluba, Melody Mimo Sithembile Maphosa, Amina Sidreck, Bles Luman, Felister Banda, Njikho Hanna

03/09/2025

GOOD MORNING TEAM.
NDIZOTHEKA KUKHALA NDI MWANA WA HIV NEGATIVE NGAKHALE MAKOLO ONSE AWIRI ALI HIV POSITIVE.

SITIKUKANA ZAWAVUTADI ANTHU AWA, KOMA ZOCHEPAZO TIZIYAMIKILA. LERO SIX LANE IJA YAYAKA MA STREET RIGHTS.SITUPANGA ZANDAL...
02/09/2025

SITIKUKANA ZAWAVUTADI ANTHU AWA, KOMA ZOCHEPAZO TIZIYAMIKILA. LERO SIX LANE IJA YAYAKA MA STREET RIGHTS.
SITUPANGA ZANDALE KOMA ZABWINO ZOKHAZO TIYAMIKILE.

02/09/2025

BOMA LIKUYENEKA KUUNIKILASO MA UFULU A ANA . MBALI YAKU HIV UKU TIKUPHWETEKANA KWAMBIRI.
MAKOLO ENAWA AZIKAKHALA KUNDENDE UKO OR TIZIKWAPULA POMPO POMPO

02/09/2025

UMUNTHU UKUTIVUTABE AMALAWI

Takumana ndi mwana wa zaka 10 . Apedzeka HIV positive lero. Kufutsa amayi kuti fotokodzani zayenda motani.
Amayi anapedzeka positive pa mimba ya mwanayu ndipo ku sikelo anabwera tsiku limodzi lomwelo basi ,ndekuti nthawi yonseyi amangokhala osamwa mankhwala . Akuti anachilila ku chipatala koma zokaikitsa.
Abwera nayo lero mwana chifukwa choti adwalika. Zilonda thupi lonse, kutupikana ku nkhope , weight loss, kakuoneka ngati wazaka 6.

Kunena chilungamo zimawawa no size ukamakumana ndi zinthu ngati izi.
Mwina ndikutheka kuti anthu ambiri uthengawu alibe okwanila? koma uyu ngati anamupedz Nako ndekuti anampatsa uthenga oyenela.

TSIKU LINA MZAMVA KUTI NDAMANGIDWA CHIFUKWA CHOPELEKA MAKOFI KWA MAKOLO OTAILILA NGATI AWA.

02/09/2025

MOYO UMAKUPHUNZITSA OKHA UKAMATAILILA. BENARD

02/09/2025

AMBIRI TIMAZILODZA TOKHA, OSANAMIDZIRA ANTHU.
UKUGONANA NDI ANTHU MOSAZITETEDZA WAYAMBA KUDWALA ATI ANDILODZA.
PITA KUCHIPATALA CHABWINO, UYO KWA SING'ANGA . KODI SING'ANGA AMAYEZA HIV?, KODI SING'ANGA AMAKHALA NDIMA ARV?
KODI SING'ANGA WANUYO ANGACHILITSE MA STI???

02/09/2025

PEPANI KUYAMBILA WEEKEND SITUKWANITSA KUPANGA ACCESS MA MASSAGES MKATIVUÑGIRA KU INBOX. WE ARE WORKING TOWARDS IT MYANKHIDWA ZONSE ZIKATHEKA

02/09/2025

NGATI SITIKULANDILA THANDIZO LA MATENDA OPATSILANA POGONANA, MTHA KUKHALA MOYO WANU WONSE OSABELEKA

02/09/2025

GOOD MORNING TEAM.
NEW DAY NEW CHALLENGES.
OSAOPA ,OSATOPA, OSAFOOKA.

GOODNIGHT FROM DRC
01/09/2025

GOODNIGHT FROM DRC

Address

Lilongwe

Telephone

+265881449676

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Fighting Against Hiv/Aids and Sti posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Fighting Against Hiv/Aids and Sti:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram