14/09/2025
Kodi ndinu mlimi ndipo mukusakasaka mbewu yabwino yoti mudzale ya soyabean?
Yankho lanu lafika gulani mbewu ya soyabean chitedze 4 , ku Renaissance Agriculture and Seed Systems Consult ndipo simudzakhumudwa
β
mbewu yocha nsanga pa masiku 90,
β
yopilira kuchilala
β
komanso mumakolola mbewu za nkhani nkhani.
πNgati mukufuna zambiri tipezeni lero ku area 25, Simama Complex room 13
Call / Whatsapp +265 995 84 08 23/
+265 999 167 703 or
Email info@renaissanceagric.com
Mbewuyi tikugulitsa pa mtengo wa MK 9,000 / kg