18/05/2022
"MA HOME REMEDIES YA MUDZI / LIKANGO /HEMORRHOIDS / PILES"
👉 Likango lilipo magulu angapo.
- Likango lotuluka thumbo koBiBila.
- Likango lam'mimba.
- Likango lam'magazi.
- Likango lina limatha kungotuluka pakhungu.
👉 Likango lomwe anthu ambiri amadwala ndi Likango lotuluka thumbo koBiBila."
👉 Komabe Likango lam'magazi komaso likango lam'mimba limathaso kusautsa anthu makamaka powafoketsa kumbali yamoyo wakugonana komaso kulepheretsa kutenga ndikupereka mimba🤰"
👉 Black seed oil komaso powder wa original amathana ndi Likango lam'magazi, lapakhungu, lam'mimba komaso lotuluka thumbo koBiBila!!!"
"KUTI MUCHILE KUMATENDA A LIKANGO PANGANI IZI👇"
1). NKHADZE."
👉 Mupeze mtengo wa nkhazi ena amati nkhadze womwe anthu ena maka m'midzi amagoba utomoni wake pochita ulimbo koma pamafunika kusamala chifukwa utomoni wake ngati utakulowa m'maso umayambitsa ng'ala ku diso ndangochenjezapo koma musaope ai pangani mosamala.
- Museme makungwa a mtengo umenewu ndiye mupsyeleretse achite makala kenako apangeni kukhala ufa ndithu mupezeso black seed oil ndikuphatikiza pang'ono ncholinga kuti angofewako pang'ono.
- Muzipaka katatu pa tsiku pali vutolo koma mutakhala pa bowo la chimbudzi munthawi yopaka yokhayi ndipo kamchira kamaduka kokha ndikuchiliratu.
- Koma ngati black seed oil simudamupeze pawokha ufa wamakala a khanzi umachizaso vutoli machitidwe ake ndi omwe ndakambawo.
2). BOWA +.
👉 Muthaso kupeza bowa omwe unamera pa mtengo uja, upsyeleletseni ndikuphatikiza black seed oil kumapaka pali vutolo katatu pa tsiku mudzachilitsidwa khulupilirani Namalenga si ine ai ndipo muzachira ndithu.
3). APPLE CIDER VINEGAR.
👉 Sakanizani teaspoon imodzi ya ACV ndi teaspoon imodzi ya Uchi mumkapu ya madzi ofunda ndi mkaka ndikumamwa kawiri patsiku musanadye kanthu.
"KENAKO"
👉 Nyikani thonje mu ACV ndikumapaka pamalopo kwinaku mukumamwa ACV yo.
– Mumva kuwawa kotsina mukangoika kumene koma pambuyo pake muyamba kuvabeino kuwawa ndi kunyerenyesa kusiya.
👉 Muzipakabe mpaka katatu patsiku mpaka paphwere.
4). MADZI OWUNDANA
👉 Ikani madzi owundana (ice pack) pamalopo kwa 30 minutes.
👉 Pangani izi kawiri patsiku mpaka muchire.
5) MADZI AM'MANDIMU.
👉 Nyikani thonje mu Lemon juice ndikupaka poBiBila.
👉 Mukuyenera kupilira kuotcha mukangopaka kenako muyamba kuva bwino.
👉 Kenako finyani ½ ya Ndimu🍋 mumkapu yodzadza ndi mkaka otentha ndi kumwa onse. Muzimwa pakapita 3 hours iliyonse.
6). ALOVERA
👉 Pakani zamkati mwa alovera poBiBila po kawiri patsiku.
👉 Ngati zapanga mkati / internal hemorrhoids. Dulani masamba a Alovera mkuonetsetsa kuti mwachotsa minga. Ikani ma slicewo mu container ndi kuika mu fridge. Akapanga freeze ikani kumaloko.
7). Muzipaka Olive Oil koBiBilako patsiku kawiri kwa tsiku lililose mpaka mutaona kusintha
8). Muzimwa ma Tambula opitilira 10 ya madzi tsiku lililose.
*"MITUNDU YA LIKANGO!!!"*
*👉 Likango lilipo magulu angapo.*"
- Likango lotuluka thumbo koBiBila.
- Likango lam'mimba.
- Likango lam'magazi.
- Likango lina limatha kungotuluka pakhungu.
*👉 Likango lomwe anthu ambiri amadwala ndi Likango lotuluka thumbo koBiBila."*
*👉 Komabe Likango lam'magazi komaso likango lam'mimba limathaso kusautsa anthu makamaka powafoketsa kumbali yamoyo wakugonana komaso kulepheretsa kutenga ndikupereka mimba🤰"*
*👉 Black seed oil komaso powder wa original amathana ndi Likango lam'magazi, lapakhungu, lam'mimba komaso lotuluka thumbo koBiBila!!!"*
*🥃LIKANGO LESSON*
⏩Ndikutupa kwa minofu ya mitsempha
↘️MITUNDU YA LIKANGO
↪️ LIKANGO LOTULUKA PAFUPI NDI KHOMO LACHIMBUDZI
↪️ LIKANGO LOTULUKA KUKALISECHE
↪️ LIKANGO LOTULUKA PAKHUNGU(nsana,pamwendo or mmaso
↪️ LIKANGO LA MMAGAZ NDI MMAFUPA
*↘️ZIZINDIKIRO*
```↘️Ululu komaso kutentha malo omwe pali likango
↪️kuyabwa pamene pakhudzidwapo
↪️kutulutsa magazi
↘️Ana akabadwa kumangomwalira(kupita padera)
↪️mayi akatenga mimba sikhala imangochoka
↘️Kudwaladwala mayi akatenga mimba( matenda achilendo)```
↘️MAGAWO A LIKANGO
↪️LIKANGO LAMKATI MWA PHUPI
↪️ LIKANGO LAKUNJA KWA PHUPI
*↘️ZOMWE ZIMAYAMBITSA*
```↪️kulera wakuchipatara
↪️kutaya mimba
↪️kusokonekera kwa mahormone
↪️kudya zakudya zosalongosoka(factory food,mafuta oundana made from animals)```
*↘️KUTHANANAZO KWAKE*
```⏩ Muvi oyang'anira suchedwa kulowa mmaso chomcho Likango njopeweka maka mukachita machawi ppl opeza thandizo la mankhwara mwansanga nkutsatira ndondomeko zonse mwadongosolo
↪️ Pezani black seed oil then dzigwilitsani ntchito mudzakudya dzanu nthawi zonse pomatha mwenzi mudzasimba lokoma
↪️pezan red onion ndikupanga cruch mukatero muzimata pali likangopo osaiwala kuvalira ngati kuli kukaliseche
↪️musinthe diet (vegetarian diet),ndikumamwa garlic juice mix with Apple cider vinegar mpaka mutachira
↪️pewan zakudya zamafuta ,nyama,eg,mkaka,shuga,mazira pamene mwapezeka ndi vutoli
↪️Ikani mu phara molinga powder ndi flaxseed powder kawiri patsiku mpaka mutachira
↪️pezan black seed pills kapena kalonji pills muzimwa kawiri patsiku osaiwala kumalimata likangolo ndi aluvera mixed with Epsom salts
↪️muzimwa tea wa polon kawiri patsiku,mutathiramo uchi mpaka mutachira.```
*💥PROCEEDINGS ON LIKANGO*
```⏩Likango ndimatenda osausa kwambili ndipo akakhalisa mwa munthu amaononga factory yapangila ana, komatu matenda amenewa munthu umachila maka akatsatira njira za chilengedwe, njirazi dzakumaliseche kapena pakhungu
↪️Pezani black seed oil ndikumapakako
↪️Pezani Olive oil nkumapaka