31/01/2026
*KODI MA ULCERS (ZILONDA ZA MMIMBA) NDI CHANI?*
✍🏻 Ma ulcers ndi zilonda zomwe zimakhala m’mimba kapena m’chipinda chomwe chimasunga za chakudya (duodenum). Zilondazi zimachitika pamene asidi wa m’mimba akuchulukira chulukila n’kuwononga khoma la chipindachi m’mimba. *(duodenum);*
*KOMA KODI MA ULCERS AMAYAMBA BWANJI?*
⏩ Ma ulcers amayambitsidwa ndi zinthu Monga izi;
👇🏻👇🏻
1. Kachilombo ka H. pylori
2. Acidi ochuluka m’mimba
3. Kumwa mankhwala ena nthawi yayitali (painkillers)
4. Kudya zakumwa zoledzeretsa,
5. Kukonda kumwa tiyi kapena khofi mopitirira muyezo
6. Kupswinjika maganizo (stress)
7. Zakudya monga nyemba,
8. Zolimba zomwe zimapala mmimba
9. Kusakonda kudya kumadzunga ndi njala kwa nthawi yaitali
*ZIZINDIKIRO ZA MA ULCERS*
- Kupweteka kapena kuotcha m’mimba maka maka mukangomaliza kudya ndiye chizindikiro chachikulu;
- Kusanza kapena nseru;
- Kulephera kukhala ndichilakolako chachakudya;
- Kufufuma m’mimba ndi mpweya;
- Kumamva kukhuta msanga ukangodya;
- Kumangoonda mosadziwika bwino;
- Kucheka mmimba mukadya zakudya zozidzira kapena zolimba;
- Kusanza magazi;
*🚨 ZOOPSWA ZAKE ZA MATENDAWA;*
❗ Kusanza magazi
❗ Chimbudzi chakuda
❗ Ululu waukulu m’mimba
❗ Ngati simulandira thandizo mungathe kuyamba khansa ya mmatumbo kothekera imfa;
*YANKHO LILI KUTI?*
Osapanga mistake yongochepetsa ululu painkillers basi ❌
Muyenera kuchiza chomwe chayambitsa vuto ✔
⏩ STC30 Ndiye yankho lalikulu lochizila matenda a Ma Ulcers; (zilonda za m'mimba)
1. Mankhwalawa Amachepetsa asidi m'mimba;
2. Amachotsa kachilombo ka H. pylori;
3. Amachiritsa zilonda za m'mimba kuchokera ku root cause;
Ndipo alibe side effects iliyonse;
Mankhwala athu amagwilitsa ntchito munthu aliyense amuna ndi akazi komanso Ana;
Ndipo ngati ndinu m,modzi amene mukuvutika ndi zizindikilo zomwe tafotokoza mu nkhani yathu, Musavutike Ndipo Osadikira kuti vuto lanu likule,
Thanzi lanu ndilofunika pa zinthu zonse zomwe mukupangazo🌱🤝
*Call Or Whatsapp*
0991932580*