Rev John Chilembwe Hospital

Rev John Chilembwe Hospital Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Rev John Chilembwe Hospital, Hospital, Phalombe DHO P. O Box 79, Phalombe.

Reverend John Chilembwe Hospital in Phalombe, Malawi, offers essential healthcare services, including maternal, child, and emergency care, improving access for local communities.

25/05/2026

🚨TIPEWE KOLERA🚨

Padakali Pano a za umuyo ali kalikiliki kufuna kuthana ndi Kolera yemwe wabuka m'boma lathu lino la Phalombe.

Tikupemphani aliyense mdera lino kuti atsate njira izi zoteteza moyo ku Kolera;

-kusamba m'manja ndi madzi oyera musanadye chakudya chanu
-kusamba m'manja ndi sopo mukatha kugwiritsa ntchito chimbudzi
-Gwiritsani ntchito chimbudzi bwino nthawi zonse .
-Imwani madzi okhawo amene ali oteteza ndi kolorini kapena waterguard
-Sambani manja ndi sopo mukasintha mwana thewera.
-Kudya chakudya chilichotentha komanso chomwe chasamalidwa bwino
Dziwani zizindikiro za Kolera :
Chizindikiro chachikulu cha kolera ndikusanza komanso kuchita chimbudzi chofanana ndi madzi a mpunga.

⚠️ Ngati mwaona munthu akuwonetsa zizindikiro izi, thamangirani ku chipatala chomwe muli nacho pafupi mukum'mwesa thanzi.

Kolera imafala ngati moto wolusa koma ndiyopeweka komanso ndiyochizika✅. Tiyeni tigwire ntchito limodzi kuti Phalombe akhale opandanso kolera👏








22/05/2026



Smile Life Insurance says it plans to partner with all district health offices to provide Group Funeral Cover policies for health workers.

The company’s Chief Operations Officer, Tumpale Sibakwe, disclosed this during the signing of a memorandum of understanding (MoU) between Phalombe District Health Office and Smile Life Insurance.

Under the agreement, about 1,089 health workers in the district will be covered under the company’s Group Funeral Cover policy.

Sibakwe said if a policyholder dies, the company will pay K1 million toward funeral expenses.

Meanwhile, Chairperson for Social Welfare at Phalombe District Health Office, Saidi Moto, described the agreement as timely.

Moto said it will help support members during funerals where administrative assistance may fall short.

By Thumbiko Nyirongo, Phalombe

22/05/2026



Smile Life Insurance Company has signed a Memorandum of Understanding (MoU) with Phalombe District Health Office expected to cover about 1,089 health workers under the company’s Group Funeral Cover Policy.

Speaking in Phalombe today, the company’s Chief Operations Officer, Tumpale Sibakwe, said that in the event of a policyholder’s death, the company will provide K1 million towards funeral expenses.

She added that the company plans to extend the initiative to all district health offices across the country.

Chairperson for Phalombe District Health Office Social Welfare Committee, Saidi Moto, described the initiative as timely, noting that it brings much-needed relief during funerals.

(by Ronnex Chiwanda -Phalombe 05/22/26)
.

Let's know about Ebola Virus
19/05/2026

Let's know about Ebola Virus

Dziwani za Matenda a Ebola
19/05/2026

Dziwani za Matenda a Ebola

19/05/2026

Health authorities in Phalombe have launched a five-day mass deworming campaign targeting bilharzia and intestinal worms among children aged between five and 14.

District Health Promotion Officer Happy Chawinga says over 127,000 children are expected to receive treatment in schools and communities from May 18 to 22.

Meanwhile, Paramount Chief Kaduya has urged parents and community leaders to support the exercise to protect children from preventable diseases.

According to the Ministry of Health and Sanitation, the first phase of the campaign is being implemented in Phalombe, Blantyre, Dowa, Lilongwe and Nsanje districts, targeting more than 1.1 million people living in high-risk areas.



📷Chawinga

Dziwani Momwe ziliri lero za Matenda a Kolera kuno ku Phalombe Pofikira dzulo pa 17 May 2026 m'mboma  lathu lino la Phal...
18/05/2026

Dziwani Momwe ziliri lero za Matenda a Kolera kuno ku Phalombe

Pofikira dzulo pa 17 May 2026 m'mboma lathu lino la Phalombe kwapeza anthu 15 odwala matenda a Kolera, zotsatira za anthu atatu zomwe zinatumidziwa ku chipatala chachikulu cha Queen Elizabeth komwe atitsimikizira Kuti ndi matenda a Kolera. Anthu ambiri omwe apezeka ndi matenda a Kolera achokera kwa Nkhulambe dera lomwe lachita malire ndi dziko la Mozambique.

Padakali pano, a za umuyo ali kalikiliki kufuna kuthana ndi Kolera . Zina zomwe zachitika ndi monga izi,kuphunzitsa anthu za kapewedwe ka Kolera,kugawa kolirini komaso kulumikizana ndi anthu akumadera kuti tithane ndi matendawa.

Tikupemphani aliyense mdera lino kuti atsate njira izi zoteteza moyo ku Kolera;
-kusamba m'manja ndi madzi oyera musanadye chakudya chanu
-kusamba m'manja ndi sopo mukatha kugwiritsa ntchito chimbudzi
-Gwiritsani ntchito chimbudzi bwino nthawi zonse .
-Imwani madzi okhawo amene ali oteteza ndi kolorini kapena waterguard
-Sambani manja ndi sopo mukasintha mwana thewera.
-Kudya chakudya chilichotentha komanso chomwe chasamalidwa bwino

Dziwani zizindikiro za Kolera :
Chizindikiro chachikulu cha kolera ndikusanza komanso kuchita chimbudzi chofanana ndi madzi a mpunga.

⚠️ Ngati mwaona munthu akuwonetsa zizindikiro izi, thamangirani ku chipatala chomwe muli nacho pafupi mukum'mwesa thanzi.

Kolera imafala ngati moto wolusa koma ndiyopeweka komanso ndiyochizika✅. Tiyeni tigwire ntchito limodzi kuti Phalombe akhale opandanso kolera👏






18/05/2026




Phalombe District Health Office has rolled out a Mass Drug Administration (MDA) exercise against bilharzia and intestinal worms targeting 127,076 children aged between 5 and 14 years.

District Health Promotion Officer Happy Chawinga says the exercise will run from May 18 to 22 in schools and communities across the district.

Chawinga has since appealed to parents, guardians and other stakeholders to ensure that all eligible children receive the medicines during the campaign period.

According to the Ministry of Health and Sanitation, Phalombe is among five districts selected for the first phase of the nationwide campaign because it continues to register cases of bilharzia and intestinal worms.

The ministry says bilharzia and intestinal worms remain a public health concern in the country due to complications associated with the diseases when left untreated.

18/05/2026

Health authorities in Phalombe District have launched a five-day mass drug administration campaign targeting bilharzia and intestinal worms among children.

District Health Promotion Officer Happy Chawinga said 127,076 children aged between five and 14 are expected to receive treatment during the exercise, which runs from 18 to 22 May.

The campaign will be conducted in schools and communities across the district.

https://www.malawivoice.com/2026/05/18/phalombe-rolls-out-mass-deworming-exercise-targeting-over-127000-children/

17/05/2026



Ofesi yoona za umoyo m'boma la Phalombe yati anthu atatu apezeka ndi nthenda ya kolera m'bomali.

Wofalitsa nkhani za umoyo m'bomali, a Happy Chawinga, ati anthuwa ndi ochokera m'dera la Nkhulumbe lomwe lachita malire ndi dziko la Mozambique.

Pakadali pano, ofesiyi yati yachilimika pa ntchito yophunzitsa anthu momwe angapewere nthendayi.

Wolemba: Thumbiko Nyirongo, Phalombe

Address

Phalombe DHO P. O Box 79
Phalombe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Rev John Chilembwe Hospital posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Category