Mankhwala a m'chilengedwe-Dr.phiri

Mankhwala a m'chilengedwe-Dr.phiri INO NDI PAGE YA DOCTOR PHIRI MWINI PROGECT YA HOCEDA HERBS, NDIMAPHUNZISA KOMANSO KUGULISA MANKHWALA chinsinsi chozama Cha mankhwala amchilengedwe

18/04/2025
Ena amandifunsa aphiri Kodi pangapezeke mtengo omwe paokha utha kuthesa mtundu ulionse WA matenda?Mwachidule ndiyankhe k...
18/04/2025

Ena amandifunsa aphiri Kodi pangapezeke mtengo omwe paokha utha kuthesa mtundu ulionse WA matenda?
Mwachidule ndiyankhe kuti mitemgo ndi yambili yali ndi mphanvi yomweyi koma mtengo umodzi osavuta kupeza omwe utha kupanga chilichonse mukufuna ndi thonje

Eya simunanve molakwika ndikunena za thonje amene mumamudziwa uja
Inuyo kupeza thonje ndiye kuti Muli ndi chipatala pakhomo palibe matenda angakanike ndi thonje
Mungofunika kupanga tiyi basi supuni imodzi ya mankhwala Mu kapu imodzi ya madzi otentha akazizizla musefe mumwe
Mupamge Izi katatu o patsiku
Mmmmm aphiri mwanena kuti matenda onde nde ngati ndi vuto lá pakhumgu momga ziphuphu ndi zilonda?eya simunalakwe ndanena kuti matenda onse nde zimakhala ziphuphu kapena zilonda tsukirani kapena sambani ndi tiyi yemweyu

Chosangalasa ndi choti ndinachilisapo matenda a água munthu wina pomgogwilisa ntchito masamba ndi mizu ya thonje
Maluwa ake ndimawagwilisa ntchito kwanbili pa azimai omwe AMAVUTIKA mmimba akamasamba
Koma ndanena kuti chilichonse ndi mankhwala nde samalani pa mafuta a nthanga za thonje ndi kulela WA azibambo moto kungomwa kamodzi Muli ndi tsiku lathunzu uma wanu sungapase mimba mzimai
Nde mmalo mokhaulisa azimai ndi kulera onyansa WA mzipatala inuyo azibambo imwani mafuta ya thonje nanunso mulereko asaaaa kumangonzunza azimai eti!

20/01/2025

KU LILONGWE TAPEZA SHOP KU AREA 49 MOTI MWEZI WA MAWA TITSEGULA MA HERBS ATHU KU LILONGWE

ndinapempha kuti mutithandizeko kupeza ka shop kakamgono ku lilongwe ndi ku blantyre titsegule shop yathu ya ma herbs ku...
06/01/2025

ndinapempha kuti mutithandizeko kupeza ka shop kakamgono ku lilongwe ndi ku blantyre titsegule shop yathu ya ma herbs kuli ziiii

Kuonjeza pakukonza kuti umuna ukhale okhota bwino komamso kuteteza mimba kuti isachoke therere limakuza tsitsiKuti zithe...
06/01/2025

Kuonjeza pakukonza kuti umuna ukhale okhota bwino komamso kuteteza mimba kuti isachoke therere limakuza tsitsi
Kuti zitheke pangani chonchi
Dulani dulani therere Itatu muike mbale muike kapu imodzi ya madzi,siyani kwa hora limodzi,mukatero sefani tikufuna madzi okhota aja nde thirani mmadzimo supino imodzi ya shuga ndi imodzi ya mafuta a ntsatsi sakanizani ikani mu mankhwala any aja atsitsi otchedwa shampoo kunena zoona muzandothokoza pa zotsatira za tsitsi lanu

06/01/2025

Minba yanu imangochoka?
Pezani therere lobala muchose nthanga zakezo kenako mukazimge musinje mupamge ufa muzimwa ngati Tiyi kawili pa tsiku
Supino imodzi mu kapu ya madzi otemtha
Mumwe kwa miyezi Itatu minha yanu siizachokanso mdipo simuzabalila kumpeni

Si zokhazo nanunso azibambo ngati uma wanu si okhota bwino komamso mphanvu zakuchipinda mzochepa pangati Tiyi omwewu

*Thesani vuto losowa magazi lero*Tikuluza achibale ambili kamba kosowa magazi nde lero aphiri abwera kuzaulula zinsinsi ...
09/12/2024

*Thesani vuto losowa magazi lero*
Tikuluza achibale ambili kamba kosowa magazi nde lero aphiri abwera kuzaulula zinsinsi zozama za mmene tingathesere vutoli
Chifukwa cha kuchuluka zochita sindikukwanisa kulemba nkhani tsiku ndi tsiku koma musachoke mgulu lino chifukwa apo ndi apo zabwino zizibwera

Mankhwala amphanvu othesera kusowa kwa magazi ndi masamba cabichi kupanga tiyi osakaniza ndi tsabola
Koma ngati mukufuna zachangu kwanbili pezani kalombo komwe pachiputukezi timati catato
Kalomboka sindidziwa kuti mu chilankhulo chanu mumati chani koma ndikuonesani chithunzi
Nde mukufunika kusinja kupanga ufa mkumamwa ngati tiyi ufawo olo kungophika mkumupasa adye odwalayo
Pa masiku atatu okha odwala apeza magazi onse omwe thupi lake likufunikira
Si zokhazo mukapangira odwala matenda ashuga mphanvu ya catato ndi yofanana ndi mapilisi otchedwa metiformin aja amene amakankha shuga kuchosa mmagazi kulowesa mmaselo athupi zikatero munthu amapeza bwino koma vuto la metiformin ndi loti amatsitsa mphanvu za kubedi mpamene catato amaonjeza mphanvu mwa odwala .pali zambili zoti ndikuphunziseni za katato koma mpata ndi ochepa ndizilemba pamgonopamgono chomwe mukufunika kudziwa ndi choti pali catato yemwe amagwa mmakungwa a mtengo woola komanso pali zija zimagwa mmasamba zonse ntchito ndi yofanana
Katato ali ndi ma protein ambili kuposa msomba komanso kuposa nyama ya mgombe katato ali ndi chilichonse chothandiza kuti munthu akhale moyo.

14/10/2024
Kupanga juisi wa mpilu kusakaniza ndi tsabola(mphilipili)mukhoza kuthesa khansa pa thupi lanu maka khansa ya mmapapu
14/10/2024

Kupanga juisi wa mpilu kusakaniza ndi tsabola(mphilipili)mukhoza kuthesa khansa pa thupi lanu maka khansa ya mmapapu

Mankhwala amphanvu othesera vuto losowa magazi mthupi ndi juisi wa kasomgo kapena tiyi wa masamba ake koma anthu anbili ...
14/10/2024

Mankhwala amphanvu othesera vuto losowa magazi mthupi ndi juisi wa kasomgo kapena tiyi wa masamba ake koma anthu anbili akumaikidwa magazi popanda kusintha mapetp ake tikuluza anthu chifukwa chosadziwa
Bip imatsika mwachangu ndi kasomgo,matenda ashuga amatha ndi kasomgo
Ngati simumudziwa kasomgo onani chithunzi

*ZOONA ZA Blackseed*Ndakhala ndikuona anthu ambili mmagulu osiyanasiyana akukanba za blackseed ndipo ambili mwa iwo aman...
14/10/2024

*ZOONA ZA Blackseed*
Ndakhala ndikuona anthu ambili mmagulu osiyanasiyana akukanba za blackseed ndipo ambili mwa iwo amangochita kukopera mmagulu Ena sadziwa zoona za blackseed
Nde sabata ino aphiri akufuna kuulula zoona zonse za blackseed monveka bwino.
Ndikupempha kuti musatope kuwerenga chifukwatu nkhaniyi ndi yaikulu KHALANI pompo

Choyanba ndibwere pa poizoni
Kodi blackseed Ali ndi poizoni iliyonse kapena ayi?
Zoona ndi zoti blackseed ndi mankhwala opamda poizoni aliyense moti ngakhale mwana wakhanda atha kumwa

Nde tiyeni pa ntchito zake

Blackseed ndi mmodzi mwa mankhwala odalilika kwanbili padziko pano pa kuchilisa matenda osiyanasiyana.

Choyamba ndinene za nkhani ya edzi yomwe anthu ambili amainena

HIV ndi virus yomwe imayambisa edzi virus yomweyi imalowa mu DNA kenako mkukapopera mpweya oipa otchedwa hiv1-integrase ndi hiv-1 protease zikatero DNA imasokonekera mkuyamba kumakomza ma selo athupi koma osakanikirana ndi ma virus ndiye kuti kulikonse kululowera maselo aja kumakhala kukulowanso fumbi loipalo lomwe pimafookesa ziwalo za thupi mkuyambisa matenda
Matenda amene amayambawo ndi omwe amatchedwa edzi
Nde munvese apapa,,edzi si matenda amodzi wina atha kukhala ndi edzi mkumangotsegula mmimba ena atha kumangodwala mwendo ena atha kumangodwala mutu
Izi zili choncho chifukwa cha komwe ma selo onyamula fumbiwo alowera

Nde blackseed akalowa mthupi amaletsa kuti virus isakanikirane ndi ma ma selo a thupi lathu motero ma virus amakhala alimobe mthupi koma Ali padera sakwanisa kufookesa thupi chifukwa amagwila ntchito pokhapokha akalamatira ku ma selo opamgidwa mu DNA
nde Ena mungafunse kuti Kodi zitatero nditayezesa magazi ndipezekabe ndi edziyo?kodi mukukumbukira kuti mzotheka anthu awili pa banja mmodzi kupezeka ndi edzi winayo ayi?izi zimakhala kuti edziyo inamulowa winayo koma ka virus kaja sikanaphulike mkuwazila funbi lija ndiye kuti popanda kuwaza funbilo munthu ukayezesa siionesa kuti uli nd8 edzi komanso suungadwale kufikira katazaphulika
Mchimodzimodzi kwa amene amamwa blackseed apapa zimakhala zovuta kuipeza edzi ngati hiv yaletsedwa kuphatikana ndi ma selo athupi koma musaone ngati mwachenjera chifukwa m***a kuyezesa lero mkupezeka kuti mulibe edzi koma tsiku Lina ka virus kaja katha kuzapezanso mphanvu mkuyamba kugwila ntchito edzi mkupezekanso

Nde Ena mungafunsebe kuti nde boma limanena zoona kuti edzi ilibe mankwala?ayi boma limanama
Ndikutero chifukwa nkhani apapa ndi yoti blackseed wakwanisa kufookesa HIV kokha kuti wakanika kuchoseratu kalomboko kuti kasapezekenso mthupimo
Ndingokuuzani pamgono kuti hiv kali ngati ka kapsules komwe mkati mwake muli fumbi ndanena lija nde kuti kagwile ntchito pa thupi lamunthu kamafunika kuphulika kuti ufawo ulowe mu DNA
HIVA ilibe moyo koma ili ngati remoti ya TV yomwe imagwila ntchito kusokoneza tv popanda moyo ife timati remoti ili ative(ikugwila ntchito )koma si yamoyo
Hhi imagwila ntchito ngat9 remoti ili ndi mphanvu mkati mwakemo yomwe imagwila ntchito ngati ma batili a remoti
Mukamwa blackseed mabatile aja amafooka mkulephera kugwilisa ntchito virus yomwe tikuiyerekezera ndi remoti
Nde ngati mabatili atha mu remoti remotiyo siigwila ntchito si choncho?tikatero timati ndi yakufa.
Mchifukwa chake aphiri amaphunzisa za erva botao kuti athese edzi
Zili chonchi chifukwa erva botao amakokolola tizilombo tonse mkukatutaya mu chipfu komanso mchikhodzodzo zikatero mumachosa HIV kudzera mu mkodzo komanso kuchimbudzi, tikayerekezera ndi remoti ija choyamba mabatile atha mphanvu ndi blackseed eti kenako erva botao wazachoseratu mabatiliwo mu remoti mukwataya kunja
Nde kukhala ndi erva botao,blackseed,Santa luzia komanso chikasu mukhoza kuthesa edzi mosavuta
Santa luzia ndi uja ena amati asthmaweed ntchito yake ndi yotsuka DNA kuti musapezeke chilichonse chonyansa.komanso amakweza chitetezo kuti kalombo kaje kafulumire kutha mphanvu

Kodi mzoona kuti blackseed angathe kufookesa HIV yense MMASIKU 45 monga amaphunzisira anthu?
Ayi
Tikutero chifukwa blackseed amathesa vuto lalikulu mkati mwa MASIKU 60 akugwila ntchito mthupi nde mukamapeza zomwe anthu akulemba zoti m***a kuthesa edzi ndi blackseed MMASIKU 45 musazikhulupilile chifukwa sayansi inavomereza za kuthesa edzi koma nthawi yodalilika ndi miyezi Iwili kapena kuposerapo

Pankhani ya ungomwa
Anthu ambili Ali ndi vuto losowa mwana ndipo ayesesa kuyenda mwa asimganga osatheka

Nthawi zambili kusowa mwana kumakhudza ma hormones
Kaya kwa mwamuna kapena mkazi blackseed akhoza kukonza vutoli modalilika
Choyamba tiyambe kwa mwamuna
Mwamuna kumwa mafuta ya blackseed 2,5ml kamodzi pa tsiku kwa MASIKU 60 azapeka kuti wakhotesa bwino umuna wake,waonjeza kuchuluka kwa umuna komanso waika mphanvu yaikulu mu umuna kuti uzikwanisa kusambila mpaka kukalowa MWACHANGU mu chiberekero

Kutsogolo kuno ndizanena za mmene umuna umalowera mchiberekero
Blackseed amapangisa kuti umuna ukhale waliwilo lalikulu pokalowa mchiberekero

Kwa mkazi
Blackseed amaonjeza kapangidwe ka mazila komanso amasamala mchiberekero kuti mphanvu yakuswa mazila ikhale yoyenerera
Pa chifukwa ichi kumwa blackseed mumathesa vuto lomasamba kawili pamwezi komanso kuchosa vuto lonva kuwawa posamba

Tibwere pa amene amabalila tsoka
Tikati kubalila tsoka tikunena za amene minba zimangochoka zokha

Blackseed amamanga mimba kuti isachoke
Kodi amamanga mpaka liti?
Blackseed anaikidwa mphanvu yoti azitha kuzindikira zoona za chilengedwe
Blackseed analengedwa mu njira yodabwisa yekha amatha kuzindikira kuti izi zikuchitikazi SI zomwe mulungu amafuna iye amapanga zomwe mulungu amafuna kuti zizichitika nde ngati mimba zanu zimachoka zokha imwani mafuta ya blackseed pomwe muli ndi mimba simuzabala nthawi isanakwane ndipo miyezi 9 ikazakwana blackseed yekhayekhayo azadziwa kuti nthawi yakwana azakonzanso zoti mwanayo abadwe

Pali kafukufuku osonyeza kuti mkazi amene amamwa kwambili blackseed atha kubala mosavuta pa miyezi 9 komanso Ena atha kupitiliza miyezi yobala mpaka kufika miyezi 12
Zili chonchi ngati mimbayo ili ndi mavuto
Blackseed akangodziwa zoti mwanayo sanakhale bwino mmimbamu amatha kuimisa mimbayo kuti isabale MWACHANGU kufikira mwanayo akonzeke moyenerera
Blackseed mmawu Ena tinganene kuti amakonda chilungamo za chibwana amakana akangoona kuti penapake sipali bwino iye amapaomgola
Izizi mzomwe zimapamgisanso kuti akaona kuti inuyo mwamwa mankhwala enaake oipa iye amatha kusukulusa mankhwalawo kuti asaononge thupi lanu
Mwachitsanzo KU India anamwesa mbewa panado wambili pa nthawi imodzi kenako chiwindi chisanasokonekere anazimwesanso blackseed patangotha mphindi 5 zokha blackseed anasukulusa poizoni yense wa panado ndipo mbewazo sizinafe ngakhale chiwindi sichinapitilize kuonongeka

Pakhansa
Blackseed ndi mankhwala achiwili odalilika pothesa khansa ya mtundu ulionse pambuyo pa nkhadzi
Blackseed amaphwesa malo otupa kenako mkubwezeresa malo oonongeka ndi khansayo mkuikapo khungu labwino

Kwa lero ndiimile Kaye pamenepa ndizapitiliza za nkhaniyi kutsogoloku koma dziwani kuti kamwedwe ka blackseed mkosiyana zimadalila matenda omwe mumthu Ali nawo nde ndizakuuzani mmene mungamwere pa matenda osiyanasiyana koma kwa lero dziwani kuti ngati ndi vuto lalikulu lomwe limatenga nthawi kuti lithe muzimwa 2,5ml ya mafuta kamodzi patsiku kapena supuni ya phala mu kapu ya madzi otentha katatu pa tsiku
Koma ikakhala vuto lomwe limatha kwa masiku ochepa monga malungo m***a kumwa masupuni awili mu kapu ya madzi otentha katatu pa tsiku kapena 5ml kawili pa tsiku
Zikunveka bwanji za blackseed?ndemanga zanu zimandilimbikisa

Endereço

Tete

Notificações

Seja o primeiro a receber as novidades e deixe-nos enviar-lhe um email quando Mankhwala a m'chilengedwe-Dr.phiri publica notícias e promoções. O seu endereço de email não será utilizado para qualquer outro propósito, e pode cancelar a subscrição a qualquer momento.

Entre Em Contato Com A Prática

Envie uma mensagem para Mankhwala a m'chilengedwe-Dr.phiri:

Compartilhar

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram