Malawi Medical Students Association -IUA

Malawi Medical Students Association -IUA Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Malawi Medical Students Association -IUA, Medical and health, international university of africa, Khartoum.

25/03/2022

Halitosis(nthenda ya kununkha kwa nkamwa)

KODI TINGAPEWE BWANJI NTHENDA IMENEYI?
1.titha kupewa nthenda imeneyi pokumana ndi Dotolo wa za Mano mwapafupipafupi..
2. Potsukitsa Mano kuchipatala
3. Potsuka Mano kawili patsiku ndi techniques yoyenela kwa phindi zokwana ziwili or zitatu
4.musaiwalenso kutsuka lilime lanu bwino ndi toothpaste chifukwa funguli kwa nthawi zambili limachokela pa lilime
5. Pewani kudya zakudya zomwe zimasiya fungo nkamwa mukadya
6. Chepetsani kudya zinthu za sugar komanso zokhala ndi caffeine
7. Imwani madzi ambili
8. Tafunani bubble gum yemwe samakhala ndi sugar mu contents yake

Hope mwaphunzilapo zingapo ndithu☺️

29/10/2021
Post Eid Celebration
16/05/2021

Post Eid Celebration

Eid Mubarak
13/05/2021

Eid Mubarak

Family
01/02/2021

Family

06/11/2020
Nurses are the heart of Healthcare
02/09/2020

Nurses are the heart of Healthcare

Its a beautiful thing when a career and passion come together @ Fatima Chitimbe from faculty of Nursing Sciences
16/08/2020

Its a beautiful thing when a career and passion come together @ Fatima Chitimbe from faculty of Nursing Sciences

Congratulations to them  MAMSA
10/08/2020

Congratulations to them MAMSA

Address

International University Of Africa
Khartoum

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Malawi Medical Students Association -IUA posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share