The Lokas Delivering Smiles

The Lokas  Delivering Smiles The Lokas is a trusted couple dedicated to delivering thoughtful and personalized gifts to friends

“Pitani ku Blantyre mukandithokozere kwa Yvone,we have been friends for a long time ndipo amandithandiza muzambiri,” Dan...
24/04/2026

“Pitani ku Blantyre mukandithokozere kwa Yvone,we have been friends for a long time ndipo amandithandiza muzambiri,” Danass said

We delivered fresh flowers as a symbol of love and cash, for safety reasons sititchula🤣🏃‍♂️🏃‍♂️

Takamupeza ku ntchito kwawo ku MBC🇲🇼

Thanks Danass for trusting the Lokas,💕💕🕺

“Mkazi uyuyu amwene anasintha moyo wanga, ndi chi support system cha Nyatwa, ndikufuna mukandithokozere ”,Alfred said👏🏻T...
18/04/2026

“Mkazi uyuyu amwene anasintha moyo wanga, ndi chi support system cha Nyatwa, ndikufuna mukandithokozere ”,Alfred said

👏🏻This evening we surprised Aunt Noria at NRC with a Birthday Cake and A bouquet of flowers from her husband and Friends respectively🎉🎉🎉💕💕

Delivery made simple, Love made visible💕✅

Inu mutituma liti. 0995108693☎️

“She might look young koma zomwe iyeyu amachita ku family yathuu eeee ndikholo, ndi mwana ozipereke munyengo zonse, pama...
16/04/2026

“She might look young koma zomwe iyeyu amachita ku family yathuu eeee ndikholo, ndi mwana ozipereke munyengo zonse, pamavuto angakhalenso pa Mtendere👏🏻👏🏻👏🏻”

This Morning , Aunt Agness Kumwenda anatituma kuti tikamuthokoze Khumbo Nyirenda pazomwe amachita. Amapanga zinthu zoposa nsinkhu wake!!

As a token of appreciation we delivered a fresh Rose flower(Symbol of Love), a Card and Cash💵

Inu mutituma liti?? 0995108693🎉

15/04/2026

Chisomo wanted forgiviness and it came to pass, she trusted the Lokas👏🏻👏🏻👏🏻👏🏻

This afternoon, Madalitso Chazima (UK based) also sent us to express appreciation to Deborah Masina, the founder of Mai ...
14/04/2026

This afternoon, Madalitso Chazima (UK based) also sent us to express appreciation to Deborah Masina, the founder of Mai Mbambande, for being a courageous young lady who is accomplishing remarkable things in caring for the elderly.

Ndi atsikana ochepa angapange zomwe iyeyu amapanga, akuyenera Maluwa adakali moyo and as an appreciation she organized lunch for all the residents👏🏻👏🏻👏🏻

Delivered by the Lokas at Dzama Village ,TA Chitukula in Lilongwe.📍

Inu mutituma liti? 0995108693☎️

“Ndinkagwira ntchito kunyumba ya Madam Adelaide ku Chilinde Newlines 2021, Koma ndinachokako nditaba zovala, since then ...
14/04/2026

“Ndinkagwira ntchito kunyumba ya Madam Adelaide ku Chilinde Newlines 2021, Koma ndinachokako nditaba zovala, since then ndakhala ndikusowa mtendere mumtima mwanga, kuimba phone samandiyankha ndiye ndimafuna mukandipepesere.

“Zovala zomwe ndinaba ndinasiya kuvala ndipo ma video omwe ndinapanga pa Tiktok nditazivala ndinadilita, ndinalakwitsa ndipo mpaka lero sindimadziwa kuti chinandinyenga ndi chani” Chisomo said

This morning tinawasaka abwana ake akale a Chisomo ndipo tawapeza ku Mchesi, ku Chilinde anasamukako👏🏻👏🏻

Chisomo wamasulidwa ndipo amukhululukira👏🏻👏🏻👏🏻💕💕💕

Chisomo gave us fresh Flowers and Money ammounting to K100,000 just to appreciate her👏🏻

Inu mutituma liti tikakupepeseleni? 0995108693📲

13/04/2026

Deliveries🔥🔥✅💕

“Nditapanga ngozi 2024 Mkazi wanga anakhala nane until i fully recovered , sindinkapanga chilichonse koma Mkazi wanga wa...
12/04/2026

“Nditapanga ngozi 2024 Mkazi wanga anakhala nane until i fully recovered , sindinkapanga chilichonse koma Mkazi wanga was there, supporting me both physically and financially !! Kupatsidwa Mwai osankhanso i will still choose her (Eunice)” Richard said.

Pitani mukandithokozere👏🏻👏🏻👏🏻

Last night, we delivered a Birthday Cake, Fresh Flowers and K1,000,000. (From Husband to Wife) and K500,000 came from a little sister Rosena Banda🔥📍

Delivery Made simple, Love made visible💕💕

Venue : New Dawn Events Centre

Azipanga surprise okha💕💕 She clearly  understands the power of self love.To celebrate her remarkable achievements and mi...
11/04/2026

Azipanga surprise okha💕

💕 She clearly understands the power of self love.

To celebrate her remarkable achievements and milestone 50th birthday, Susan treated herself to a cake, fresh flowers, and a luxurious spa experience at Umodzi 5-Star Hotel.

She entrusted us with delivering this special surprise, and we were honored to be part of such a meaningful occasion.

08/04/2026

The surpriser was surprised 🙌🏻🙌🏻🙌🏻🤣

Ma guys a ku Linga FM mwawina🤣🤣

“Tamandani was there for me when Heartbreak newly took my life, he gave me both financial and spiritual support.“Uyuyu a...
07/04/2026

“Tamandani was there for me when Heartbreak newly took my life, he gave me both financial and spiritual support.

“Uyuyu analipilirako ana anga fees zinthu zitafika pothina, uyuyu anandilipilirapo rent Landlord atamenyetsa nkhwangwa pa mwala kuti ndituluke”
Mumie Malawi said 🔥🔥🔥🔥🍦

Sindingakwanitse kumuthokoza, pitani mukandithokozere👏🏻👏🏻👏🏻👏🏻👏🏻

We delivered 🎉 Samsung S22 Ultra, Screen Protector, Porcher,Apple Beats, Fast Original Charger, Fresh Flowers, Water resistant Smart watch,

Delivery made simple,Love made visible🎉🎉🎉🎉

Happy Birthday Tamandani Nkhata🎉🎉🍦and thanks Mummie Malawi for trusting the Lokas👏🏻👏🏻👏🏻

“Ndinali paubale wabwino ndi sister wake , first born wa kwawo, ndiye poti sister wakeyo anamwalira, mukandithokozere kw...
05/04/2026

“Ndinali paubale wabwino ndi sister wake , first born wa kwawo, ndiye poti sister wakeyo anamwalira, mukandithokozere kwa Brother wakeyo”

“This guy is a Mechanic and very hardworking and i want to support his business in absence of his Sister” DRdee NyaChirwa said💕💕💕

It was very emotional🙌🏻 wait for the Video🎉🎉

Arthur tinakamupeza ku Garage kwake ku Kanengo📍✅

Thanks for trusting us Madam Danass🕺🕺

Address

2 Kwartel
Cape Town
7560

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The Lokas Delivering Smiles posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share