Namkungwi Green World Clinic

Namkungwi Green World Clinic Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Namkungwi Green World Clinic, Pharmacy / Drugstore, 7oakmere a. h/golden Highway, Johannesburg.

04/09/2022

Hello my people how are u doing

28/07/2022

*Hi Anamkungwi*

LELO TIKAMBE IZI👇👇

*1. KUSATENGA MIMBA*

*2 KUPANGA PERIOD KAWILI OR KATATU MWEZI UMODZI*

*3 ZOTUPA ZA CHIBELEKE*

NB : pali me ZIMAI safuna kutenga mimba aliyense amafunitsitsa a Kuakhala ndi phaso yamwana ndipo zimangoona kuvuta koma mwa ndizonyadilitsa kwambili.

*KUSATENGA MIMBA*

Masikuanu mzimai kulephela kutenga mimba sizitathauza kuti muthu ndi osabeleka ai pali zifukwa zambili zomwe zimachititsa mkazi kuti asatenge mimba monga👇👇

1. Zotupa zamimba : thawi zambili zotupa za chibelekelo zimalephelesa mzimai kutenga mimba chifukwa umuna sudutsa bwino bwino ndipo umavutika kukakumana ndidzila la ZIMAI...

Azimai omwe Ali ndivutoli period Yao I makhala yovuta kwambili amasithasita modabwitsa kwambili ndipo amavakuwawa enaso kukomoka kumene😳.

Ena amatha kupanga kawili koma period yachiwilio eeeh imangotuluka pang'ono komatu I makhala yowawa zija zoti sangadzuke....

NGATI MULI NDI VUTO LIMENELI YESANI KUPEZA MAKHWALA AWA👇👇

*UTERUS CLEANSING PILLS*

Awawa ndi ma pill omwe a makhala ndi Kachingwe komaso mkatimo so mumakhala ma grov omwe umagwilitsila ntchito Kulowetsa kundata ndipo pill imenei imakhalaso ndi kachigwe.

Pills imenei imakoka zoipa zonse mkati mwa chibelekelo ndipo zotupa zonse zimatha ndimakhala othandiza kwambili..

Chithuzi chamakhwalao ndiawo alipasio.

Muthaso kuonela vedio mwambamo

*Thawi yamafunso*

ANANKUNGWI  GIVE FOR GIVERS ↘️ We Helps couples  to understand  there  marriage  problems  and teaching how handle  the ...
10/12/2021

ANANKUNGWI GIVE FOR GIVERS

↘️ We Helps couples to understand there marriage problems and teaching how handle the peacefully

↘️We sell Natural Herbs which there dillu with different disease like

↘️Chlamydia
Ge***al herpes
Gonorrhea
HPV
P***c lice
Syphilis

Trichomoniasis

Heart disease

Cancer

Unintentional injuries

Chronic lower respiratory disease

Stroke and cerebrovascular diseases

Alzheimer's disease

Diabetes

Influenza and pneumonia

Kidney disease

Su***de

Address

7oakmere A. H/golden Highway
Johannesburg

Telephone

+27681146435

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Namkungwi Green World Clinic posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Namkungwi Green World Clinic:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram