25/06/2024
Takulandilani pa bwalo lino pomwe mudzipezapo zoona zokhazokha za nkhani m'banja kapena chibwenzi... Anthu ambiri timanamizana tikakhala pa maubale oterewa.. Koma pali zoona zenizeni zomwe zimachjitika mkatikatimo... Uzani amzanu k*t apange follow page ino k*t uthengawu usawaphonye... Mabanja alimbe pouzana zoona zokhazokha...