Healthwise with Kittah

Healthwise with Kittah โœ“ Registered Pharmacy personnel๐Ÿ’Š
โœ“ Professional Health Educator๐Ÿ’‰๐Ÿฉบ

โš ๏ธThis page is for Educational purposes only.

Go to the Hospital and Get checked.!!
๐Ÿ’Œhealthwisewithkittah@gmail.com

๐Ÿคง๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚
13/05/2026

๐Ÿคง๐Ÿ™Œ๐Ÿ˜‚

Iwenso ??๐Ÿ˜…๐Ÿ˜‚
13/05/2026

Iwenso ??๐Ÿ˜…๐Ÿ˜‚

MA EMERGENCY PILLS: 1. Amagwira ntchito mukamwa within 3 days (72 hrs) after S3x.Nde pali ena amatha kugwira ntchito up ...
09/05/2026

MA EMERGENCY PILLS:
1. Amagwira ntchito mukamwa within 3 days (72 hrs) after S3x.
Nde pali ena amatha kugwira ntchito up to 5 days (120) after S3x.

2. Sitimweratu before S3x, Chifukwa chokuti amayamba kugwira ntchito nthawi yomweyo mukamwa, ndye mphamvu imayamba kutsika as time goes.

3. Emergency pill Samachotsa mimba ngati mwamwa muli kale ndi mimba.

4. Samateteza ku ma STIs

Ngati pali mafunso ena alembeni mu comment section.๐Ÿ˜Š
ZIKOMO.

Nde mwati kwabwera kachifuwa kosachidzika ?Nde mkumatanino anzanga ?
09/05/2026

Nde mwati kwabwera kachifuwa kosachidzika ?
Nde mkumatanino anzanga ?

17/04/2026

Munadziwa bwanji kuti LABOUR yayamba, m***amangire kuchipatala ??
Tiphunzitseni mu comment section ๐Ÿ‘‡

15/04/2026

Azibambo iyiyi its a Must muwonere.
How to Support your wife ku Labour ward

06/04/2026

Ma Mistakes amene mkupanga ndi awa,
Ma ulcers a m'mimba ndi zilonda zoti zimapola ndithu koma osati mophweka.
Yetsetsani kuti mkupewa ma mistakes awa.

As you grow old its time yoti you take your diet very seriously because your body is slowing down.

SHARING IS CARING Osaiwala ๐Ÿ˜Š๐Ÿ™

You got this ๐Ÿค—๐Ÿ˜€๐Ÿ”ฅ
13/02/2026

You got this ๐Ÿค—๐Ÿ˜€๐Ÿ”ฅ

26/12/2025

Njira zolerera za pa mkono.
Wonerani Video lesson iyi kuti Mudziwe za Njira za pamkono zimene zimapezeka kwathu ku Malawi kuno, Monga:
- Jadelle wa 5 years
- Levoplant wa 4 years
- Implanon wa 3 years

Njira izi m***a kuchotsa nthawi iliyonse mkufuna kukhala ndi mwana, kaya mwakhala nacho dzaka ziwiri or chimodzi, m***a kukachotsetsa ndikukhala ndi mwana bwinobwino.

mkaikitsa mmayenera mudikire matsiku 7 kuti chapamkono chiyambe kugwira ntchito.
m***a kupewa kugonana panthawi iyi, kapena m***a kugwiritsa ma condom panthawi imene mwaikitsa chapamkono mpaka padutse matsiku 7.

@topfansMinistry Of Health - Malawi

20,000 people choosing health knowledge over myths.This page exists to simplify health, prevent complications, and save ...
14/12/2025

20,000 people choosing health knowledge over myths.

This page exists to simplify health, prevent complications, and save lives through education.
Thank you for trusting Healthwise with Kittah. More value coming.

Mu ichichi tili Limodzi ๐Ÿ”ฅ๐Ÿ’Š๐Ÿฉบ

21/11/2025

Nthenda Ya ma Ulcers Ndiyochizika Ndithu.
WATCH THIS VIDEO MODEKHA KUTI mudziwe kuti mungapange bwanji mkadwala ma ulcers.

Munthu sumachila pompo pompo, But it can take 3 weeks to 4 months kuti muchile ma Ulcers IF AND ONLY IF You follow Malangizo akuchipatala, Dose yonse mwamaliza komanso Diet ndi Lifestyle ili yolongosoka.

Address

Lilongwe
B1

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Healthwise with Kittah posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Healthwise with Kittah:

Share