
05/07/2024
*NKHANI YABWINO KWA TONSE*
tidziwe za mbewu za F1.
mwinatu ena mumangongomva kuti mbeu za F1.
Izizi ndi mbewu za hybrid zomwe zimapangidwa mosiyana ndi zinzake za hybrid.
Hybrid alipo wambiri koma si yense yemwe ndi F1.
*Kodi ubwino wa mbewu za F1 ndi wotani?*
1.zimacha nsanga,mwachitsanzo, tomato wa f1 amacha masiku pakati pa 70 ndi 80 kuchokera pa tsiku lowokera.
2:zimalimba kwambiri ,siziola msanga, mwachitsanzo, TOMATO wina wa f1, amatha kukhala mwezi asanaole, kuchokera tsiku lomwe wacha.
3:Zimabeleka kwambiri,umathyola kwa nthawi yaitali:mwachitsanzo, TOMATO wambiri wa F1, akayamba kucha, umathyola miyezi yochuluka,pakati pa 4 ndi 8,kutengera mmene wasamalira.
4:zimapilira ku matenda ambiri omwe mbeu zinzake zimagwidwa nawo mwachitsanzo, tomato wa BAWITO F1, amalipira ku matenda aja a kafota.
5:Zimakhala za kolite/high quality,zolimba.
6:umapeza phindu Chifukwa chakuti Zimabeleka nthawi yaitali,ndiye olo kubwere mpweche,iweyo umakolola mpakana mpwechewo kutha,kulowa mu season yosowa mbeuzo.
7:zimasowa,nde aliyense.akudziwa kuti Chinthu chosowa chimakhala chabwino.
8:amabeleka kwambiri,ukasamala,bunch Imodzi mpakana zipatso ten.
Apa m***a kuona kuti ubwino wa mbeu za F1, ndi wambiri.
Tsopano tikukudziwitsani kuti tili ndi mbewu ya TOMATO,F1 ,wampaketi,wogulitsa,pa mtengo wotsika,kuti aliyense amene akufuna kuyesa kulima F1,alime.
Tili ndi tomato wa F1,BAWITO F1
MU packet IMODZI ya 5g muli mbeu 500 pa mtengo wa k29,000.
Nde kuti mbeu 1000,ndi k58,0000.
Ife tili ku Blantyre, timatumizanso kulikonse
Mu Malawi muno mwa ulele.
Dziwani kuti kulima tomato wa F1 ,ndie kuti wathana ndi za mpwechezi, chifukwa ukolola mpakana kudzakumana ndi chithumba.
Tomato wa f1 wa BAWITO umayamba kukolala pakatha 75 days from transplanting,ukatero kukolola mpakana miyezi
Yosachepera 4,yosaposela 9 kutengera mmene wasamalira.
Tiyankhuleni pa 0999420917.
Tomato wa F1 waphweka tsopano!!
BAWITO F1!! muyeseni!!
Uyu mukafetse nokha !!
Ngati kufetsa kumakuvutani, tikupatsani upangiri waulele.