
07/01/2023
*VUTO LOYIWALAYIWALA / KUBALALIKA / MEMORY LOSS*
Vutoli ndi kuyiwala kodza mosadziwika bwino. Munthu amatha kuyiwala zinthu zangochitika kumene kapena zakale penanso zonse.
Vutoli limatha kukhala lakanthawi kochepa kenako kapena loyambiranso komanso lanthawi yaitali molingana ndi chomwe chayambitsa vutolo.
*Mayina ena avutoli;*
Forgetfulness, Amnesia, Impaired Memory, Loss of Memory, Amnestic syndrome, Dementia-memory loss, Mild Cognitive impairment- memory loss
*ZOYAMBITSA*
1. Kukula
2. Kuvulala kwa ubongo
3. Zotupa zamuubongo
4. Pochidza Cancer
5. Kusafika kwa oxygen okwanira ku ubongo
6. Kuvulala kwa mutu
7. Nthenda yamuubongo
8. Kudwala nthawi yaitali
9. Surgery
10. Stroke
11. Kudzadza kwa madzi mu ubongo
12. Nkhawa
13. Kubalalikabalalika
14. Mowa
15. Kugwiritsa ntchito mankhwala ozunguza ubongo
16. HIV/AIDS
17. Kugwiritsa ntchito mankhwala nthawi yaitali
18. Kuchepa kwamavitamin B muthupi ( Vitamin B1, Vitamin B12)
*Chitsamaliro chapakhomo*
Munthu yemwe akuyiwalayiwala amafunika chitsamaliro chachikulu.
1. Kumawaonetsa zinthu zosavuta kudziwa, nyimbo komanso zithuzi zodziwika mosavuta.
2. Kumawalembera nthawi yoyenera kumwa mankhwala or kuchita chinthu chilichonse chofunika.
3. Ngati munthuyo akufunika chitsamaliro tsiku lililonse komanso thanzi lawo sililibwino pakuyenera kuyamba chitsamaliro chapakhomo chitsamalira odwalayo tsiku ndi tsiku.
*Mankhwalawa opangidwa kuchokera ku zitsamba*
Tili ndi mankhwala opangidwa kuchokera ku zitsamba a *Himalaya Mentant tablets*
Mankhwalawawa amathandiza kuthana ndi vuto loyiwalayiwala, kupangitsa munthu kuphunzira zinthu mosavuta, kukhala wachidwi, kuthetsa kubalarika komanso kuthandiza kubwezeretsa nzeru zamuubongo.
Botolo la 60 tablets @ K12,000.
Himalaya Limbe shop ili pa Phalombe Hardware mu building ya Masha-Allah Merchandise Mart ground floor room ITN28. Opposite Standard Bank
Helpline; 0884717200 /0998033132