Dolo Ozitsata

Dolo Ozitsata Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Dolo Ozitsata, Medical and health, Blantyre.

A platform for open & exciting discussions on VMMC to increase knowledge levels of the service among young and older men & their partners, while providing accurate & up-to-date information on VMMC and other sexual & reproductive health related issues.

09/06/2021
08/01/2021

Madolo!? Chaka mwachiyamba bwanji ??

31/07/2020
Madolo eni eni amadziwa kufunikira kosamala moyo wao. Amakhala omasuka ndi olunjika pa zokhumba zao zachitukuko komaso z...
30/07/2020

Madolo eni eni amadziwa kufunikira kosamala moyo wao. Amakhala omasuka ndi olunjika pa zokhumba zao zachitukuko komaso zaumoyo, choncho amakhala otsogola,

Ozitsatawo amasankha mdulidwe wakuchipatala. Nanuso mungathe kutero lero.



Tiimbireni foni pa nambala iyi 0999238328 kuti mudziwe zambiri

Inde  !  Tsopano zikutheka kulandira mdulidwe wa kuchipatala pa weekend ngati lero mu zipatala zathu za ku Limbe, Chemus...
25/07/2020

Inde !

Tsopano zikutheka kulandira mdulidwe wa kuchipatala pa weekend ngati lero mu zipatala zathu za ku Limbe, Chemusa, Gateway (pafupi ndi chipatala cha Queen Elizabeth) ndi South Lunzu (Machinjiri) mu mzinda wa Blantyre.

Kuti mudziwe zambiri imbani phone pa 0999238328.

Ndondomeko zopewera kufala kwa Covid19 zidzatsadidwa.

Khalani , Landirani wakuchipatala waulere.

26/03/2020
Anyamata ndi azibambo a mu Blantyre,Dziwani kuti m***a kulandira mdulidwe muzipatala zathu zomwe zili mmadera omwe alemb...
26/03/2020

Anyamata ndi azibambo a mu Blantyre,

Dziwani kuti m***a kulandira mdulidwe muzipatala zathu zomwe zili mmadera omwe alembedwa pa postayi.

Landirani mdulidwe wakuchiptala, Khalani Otsogola.

04/02/2020

Our war is against health inequities that keep people vulnerable to new HIV infections.

If we have to win the battle, we need to fight back and make headway in averting new infections by taking advantage of the treatments that can make the virus undetectable and untransmittable



UNAIDS UNAIDS Eastern and Southern Africa UNICEF Malawi USAID Malawi Malawi National AIDS Commission Community Initiative for Social Empowerment πŸ…²πŸ…ΈπŸ†‚πŸ…΄ Youth Response for Social Change-YRSC Life Concern Organisation Centre for Youth and Development East and Southern African Youth Alliance on SRHR and HIV Youth Initiative for Community Development-Malawi Amref Health Africa The VMMC Project at PSI/Malawi

11/12/2019

Osalubwalubwa: Khalani otsogola, landirani mdulidwe wakuchipatala lero.

Address

Blantyre

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 07:00 - 18:30
Wednesday 07:00 - 18:30
Thursday 07:00 - 18:30
Friday 07:00 - 18:30
Saturday 07:00 - 17:00

Telephone

+265999238328

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Dolo Ozitsata posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram