Care MW

Care MW WhatsAp +265999376652
(4)

careMW󱢏
"Timaphunzitsa kapewedwe ka matenda osiyanasiyana,muli phee kunyumba kwanu"
" ONCE YOU SEE THIS FOLLOW THE PAGE"
"INVANI ZOONA ZOKHUZA KUCHIPATALA "
"KUCHIMAKE KWA UPHUNGU WAKUCHIPATALA "
👉caremw217@gmil.com.

03/05/2026

🚨🚨🚨PANANGOCHITIKA KA MISTAKE PANG'ONO TINAYIWALA:
Happy Labour day kwa nonse mumawachapira ma dokotala coat 🧥 and anamwino uniform. We recognise your efforts

03/05/2026

Macheza anj awa 😧 team chipatala?

in case you missed it 🚨"🤞sikofunika mpaka achipatala akuuzen ma panti Anu aziyikidwa chonchi,onesesan kuti mwasita musan...
03/05/2026

in case you missed it 🚨"🤞sikofunika mpaka achipatala akuuzen ma panti Anu aziyikidwa chonchi,onesesan kuti mwasita musanawavale 🫡

03/05/2026

Pali ma umboni oti Malo awa 👉Blantyre,
Lilongwe komanso
Mchinji District kuli chindoko osati masewera Kaya bwanj Kaya 🥹?

in case you missed it 🚨 mayeso anzathu aja a tiwili masana tiwila madzulo atuluka 🎉 congratulations
03/05/2026

in case you missed it 🚨 mayeso anzathu aja a tiwili masana tiwila madzulo atuluka 🎉 congratulations

03/05/2026

matenda omatupa nsagwada aja kwathu kuno ayamba kumapezeka kwambiri Kaya bwanj 🥹

03/05/2026

In case you missed it 🚨 pa nkhani ya umuna wa madzi

゚viralシ ゚

03/05/2026

Mwazuka bwanj 🤩

02/05/2026

kungotenga mimba Lero ndekuti January muzakhala mwayamba kuyamwisa 🥶

02/05/2026

Kwathu nde zimakhala zima grinder zazikulu mistake pang'ono 😧

゚viralシ ゚

Winayo bambo Ake winanso bambo Ake anabadwa tsiku limodzi kwa mayi modzi anangosiyana mphindi chabe ma twins awa🚨
02/05/2026

Winayo bambo Ake winanso bambo Ake anabadwa tsiku limodzi kwa mayi modzi anangosiyana mphindi chabe ma twins awa🚨

BREAKING NEWS,🚨 NKHANI YATSOPANO PA NJIRA ZOLETSA KUTENGA MIMBA KWA AMUNA 🚨Njira yatsopano yoletsa kupeleka mimba kwa am...
02/05/2026

BREAKING NEWS,🚨 NKHANI YATSOPANO PA NJIRA ZOLETSA KUTENGA MIMBA KWA AMUNA 🚨

Njira yatsopano yoletsa kupeleka mimba kwa amuna yotchedwa ADAM yawonetsa kugwira ntchito mpaka 100% kwa zaka pafupifupi 2 m’ma trial oyambirira.

Njirayi imagwiritsa ntchito gel (hydrogel) yopanda mahomoni yomwe imayikidwa mu vas deferens kudzera mu njira yosavuta komanso yachangu ya kuchipatala.

🔬 Imagwira bwanji ntchito?
Gel imeneyi imakhala ngati chotchinga cha umuna (s***m) kuti usamayende ,

Koma

Sikusintha kumva kukoma pa nthawi yogonana
Simalephelesa amuna kuthila(ejaculation)

📊 Zotsatira zake ndi izi:
Imagwira ntchito mkati mwa masiku 30
Yaonesa 99.8% mpaka 100% kuchepa kwa kuyenda kwa s***m
Imatha kugwira ntchito kwa miyezi zaka 2 ziwiri
Palibe zovuta zazikulu za thanzi zomwe zapezeka mpaka pano
Imasinthika (reversible) — gel imasungunuka yokha ndipo kubereka kumabwerera mwachibadwa

Mosiyana ndi ma condom kapena vasectomy (yokhalitsa), ADAM imapatsa amuna njira ya nthawi yayitali kugwilitsa ntchito koma yosakhalitsa

, kuwapatsa ufulu wambiri pa za kubereka amuna anu.
Mayesero a Phase 2 ayamba kale, ndipo izi zikusonyeza kuti mtsogolo njira zoletsa mimba zingasinthe kwambiri padziko lonse.

Ikakhazikika kwathu kuno izabwela ndithu azibambo nawo azizatenga kalera wawo uyu koma mwakonzeka?

Address

Area
Blantyre

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Care MW posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to Care MW:

Share