03/12/2024
*VUTO LA KUSABELEKA KWA MAYI*
Uwu uli ngati mtanda wina umene tauwomola kuchokera muchi safuliya chija chotchedwa, Thanzi La Kuchipinda Vs La Thupi Lonse.
Masiku ano azimayi ambiri akungoleka kubelaka, ngakhale ali woti anabelekapo mwana mmodzi, kaya awri etc. Ndipo zikuchulukila.
*KODI NCHIFUKWA CHIYANI?*
Pali zifukwa zingapo monga izi;
👃 Ngati pochira before, ziwalo zina zofunika zinawonongekamo
👃 Anatengapo matenda opasilana pogonana
👃 Opalesoni yokhudza ubeleki or zifukwa zina, sinayende bwino
👃 Wakhala ak*taya mimba zoti zakula kale
👉 Kutsekeka kwama Ovarian Tube.
👃Ma fibroids mchbelekero
*KUTSEKEKA KWA MA OVARIAN TUBE*
Lero bwanji tikambepo zambiri za nkhani imeneyi. Zadziwika k*ti kusabereka kwa azimayi ambiri, mwa zifukwa taziyala zija, koma ichi ndiye chili patsogolo zeeeedi.
Ma ovarian (fallopian) tube zili ngati ma paipi amene mmene ma s***m amadutsamo, pokapanga fertilize dzila. Ndimo mmena dzila limadutsamo k*tssikila mchibelekero. Ma paipi amenewa akatsekeka, ndiye k*ti ma s***m sangadutsemo kupita ku dzila; nalo dzila lilibe kodutsa k*ti lipite mchibelekero.
*CHIMACHITISA NCHIYANI?*
👃 Ngati mchuuno muli motupa
👃Ngati mchibelekero muli ma fibroids
👃 Ngati watenga matenda opasilana pogonana
Ngati dzila llina lake linatsikila kunja kwa chibelekero
👃 Ngati opaleshoni ina yake inalakwika
👃 Ngati mma paipi mwadzadza minofu ya abnormal or ziphala zolenda.
ZOONSE tatchulazi ndizo zimapangisa k*ti ma paipi atsekeke.
*ZIZINDIKILO*
👃 Kusatenga mimba
👃 Kupweteka pansi pa mchombo
👃 Kundata k*tuluka zimadzi zosadziwika
👃 Mutu kuwawa
👃 Msana, Khosi
👃 Kutentha thupi nkumamva mphepo
👃Nselu
👃 Kumva kupweteka ku ndata pogonana.
*THANDIZO*
👉 Tea wa adyo powder + jinja powder
👉 Ma excersise
👉 Kumadya za vitamin C wambiri monga magwafa, papaya, malambe, bwemba, tea wa masamba a magwafa, za mgulu la maolanje
👉 Turmeric ~ Ka teaspoon kachitsulo kaja kamodzi mmawa, kena madzulo, kwa mwezi umodzi.