Youth counseling

Youth counseling Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Youth counseling, Blantyre.

29/01/2024

Am great and you there

02/12/2023

Everyone

06/09/2023

Today's Topic
Cultural practice and sexual immorality
Zikhalidwe zambiri my Africa zimalimbikisa mchitidwe ogonana pakati pa amayi ndi abambo komanso anyamata ndi atsikana.pachifukwa ichi anyamata ndi atsikana amakula akuziwa kale zokhaza thupiwo (sexuality).anyamata amatenga atsikana ngati chida chowasangalatsa muzilakolako zawo.
Izi ndi Zina mwa zikhulupiriro:
1.kubeleka motetezeka.
-Atsikana amauzidwa kuti ngati sakuchita mchitidwe ogonana adakali achichepele ,mafupa awo am'mahipi alimba kotero sadzakwanisa kubeleka bwinobwino mwana wawo oyamba.Ili ndi bodza kuchokera kwa satana,chifukwa Pali azimayi ochuluka omwe adakwatira Ali ma virgins ndipo adabweleka bwinobwino Ana awo onse.
2.Kufunafuna vitamin k.
-Atsikana amauzidwa kuti akuyenera kupeza vitamin k kuchokera kwa anyamata kapena azibambo,zimene amayi zimapezeke mu umuna,pofuna kuchotsa ululu mu Nthawi ya nsambo.ilinso ndi bodza chifukwa vitamin k samapezeka mu umuna koma muzamasamba (vegetables )kapena amaikidwa mthupi ndi bakiteriya.
3.kukhala ndi ma hip aakulu
-Ndi chikhulupiriro pakati pa atsikana kuti kugonana kumawapangitsa kuti akhale ndi ma hip abwino size 8,Mutha kuzindikira kuti masiku ano nkhani yokhuza ma hip yavuta kwambiri pakati pa azimayi.zafika poti Ena akumamwa mankhwala.
Izi ndi Zina mwa zikhulupiriro.
Comment and send your feedback to my inbox.

05/09/2023

Today's topic
Kupeleka ndi kulandira chikondi.
Mulungu amangitsira banja anthu a pa okha;atulusa amndende alemerere,koma opikisana naye akhala mdziko lopanda madzi (masalmo 68:6)

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Youth counseling posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram