
05/09/2025
Throughout August, our Umoyo N’kukambirana radio program focused on Pneumococcus bacteria: what it is, the diseases it causes, how it spreads and ways to prevent it. We sincerely thank all our listeners for engaging with us on this important topic.
As we enter September, our attention shifts to another critical issue: climate change and its impact on health. Starting this Saturday, climate change experts will join us to unpack how it affects health in Malawi, who is most at risk and the key measures we can take to mitigate its effects.
Tune in to Times Radio this Saturday from 5 : 00PM to 6:00 PM for this enlightening discussion.
--------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------------
Mwezi wa August, program ya Umoyo N’kukambirana takhala tikufotokoza zambiri za bakiteriya ya Pneumococcus monga matenda omwe amadza kamba ka bakiteriyayi, momwe matendawa amafalira komanso momwe tingawapewere .
Tithokoze omvera athu pokhala nafe mu nthawi imene timakambirana nkhani imeneyi.
Pano poti talowa mwezi wa tsopano wa September, tikhala tikukambirananso mutu wa tsopano- Kusintha kwa nyengo ndi zotsatira zake pa Umoyo wa anthu.
Mawa, akatswiri owona za kusintha kwa nyengo akhala akutifotokozera kuti kusintha kwa nyengo ndi chani, momwe kusintha kwa nyengo kumakhudzira miyoyo ya anthu ku Malawi, anthu amene ali pachiopsezo chachikulu komanso kuti anthu angatani kuti akhale otetezedwa ku mavutowa.
Tcherani wayilesi ya Times loweruka nthawi ya 5: 00 PM - 6: 00 PM madzulo.