Limbe VMMC Clinic chipatala cha m'dulidwe wa a bambo cha Limbe

Limbe VMMC Clinic chipatala cha m'dulidwe wa a bambo cha  Limbe Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from Limbe VMMC Clinic chipatala cha m'dulidwe wa a bambo cha Limbe, Medical and health, Blantyre.

13/12/2024

Accept the challenge get circumcised today

11/12/2024

Mwadzuka bwanji nonse ife a m'dulidwe wa abambo wakuchipata tikukulimbikitsani nonse amene munathandizidwa kale service ya m'dulidwe kt muwalimbikitseso amzanu ndikuwadziwitsa za ubwino wa m'dulidwe kt nawoso atenge nawo mbari zikomo

08/12/2024

Kwa amayi amene mumafuna amunanu atathandizidwa nawo service ya m'dulidwe mungathe kuwalimbikitsa okondedwa wanu kt nawoso atenge nawo mbari ,kmso mwina mukufuna kudziwa kt zimakhala bwanji abambo akapanga m'dulidwe mungathe kutifikila ku inbox kwathu zikomo

08/12/2024

Kd mumafuna mutalandila m'dulidwe km momakhala ma dela awa chikwawa, nsanje mulanje , m'deka,zalewa,phalombe,ndi madela odzungulila km mumafuna mutathandizidwa m'dulidwe wa kuchipatala km simukudziwa kt mungathandizidwe kt tiyakhuleni ku inbox kwathu tikuthandizani masiku amene timakhala tikuthandiza anthu mma m'dela ngt amenewa zikomo kwambiri.

21/11/2024

Kwa nonse omwe mumafuna mutathandizidwa m'dulidwe weekend ngt muli ndi mafuso tifuseni ngt muli ndi mafuso weekend kumakhala kotsegula Friday and Saturday

18/11/2024

Kd chimakufooketsani ndi chiyani kt musapangitse m'dulidwe tiyakhuleni ku inbox kwathu tikambitsane ngt Pali Zina ndi Zina zomwe mumafuna mutadziwa zokhudza m'dulidwe.

18/10/2024

I am your guy
Ndifuseni lelo za m'dulidwe

15/10/2024

Happy mother's day to all mother's
God bless you all

09/10/2024

Mwadzuka bwanji abale ndi alongo mongokumbutsana m'dulidwe wa abambo ukupitilalabe, Auzeni amzanu awawuze amzowoso amene sanathandizidwe kt m'dulidwe wu ndiwawulele . Ngt mukufuna kudziwa zambiri tiyakhuleni ku inbox kapena tiyimbileni phone or ku what's app tikuthandizani zikomo.

10/09/2024

If they don't see the value of having you, don't try to convince them.

Address

Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Limbe VMMC Clinic chipatala cha m'dulidwe wa a bambo cha Limbe posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share