10/08/2025
🔸Kodi munasiya school kalekale koma mumafuna mutalowaso mclass? Kaya ndi primary kaya secondary?
🔸Kodi mukufuna mutaphunzira kulankhula English?
🔸 Mukufuna mutaphunzira njira zamakono zopangira business?
Yankho lanu lafika lero ndi Wills online Academy m***a kuphunzira zosezi muli kwanu kudzela pa phone yanu yammanja pa mtengo otsika kwambiri
Lembetsani lero potipeza pa Whatsapp kapena kuimba ma nambala awa 0881390951 kapena 0990388912
Timapelekaso guidance and counseling ngati mwakumana ndi mavuto osiyanasiyana