Vujah The Community Health Nurse

Vujah The Community Health Nurse This page is aimed at sharing Information that will help in promoting health and preventing Diseases

15/08/2024

Did You know?

Munthu akavulala spinal cord (Spinal cord Injury) palibe thandizo la chipatala limene lingaperekedwe k*t akhalenso wa lunga...
Best way ndikupewa basi.

No child is safe from polio paralysis until every child is vaccinated. I support polio vaccination because it’s the only...
07/12/2023

No child is safe from polio paralysis until every child is vaccinated. I support polio vaccination because it’s the only way to protect children from a deadly disease and give kids a chance at a healthy life.
.

14/11/2023

14 November every year is

Here are some ways how we can prevent diabetes
1. Loose extra weight if you are over weight
2.Quit your Sedentary Lifestyle and get moving
3.Eliminate refined carbohydrates, sugars and processed foods from your diet
4.Switch to healthy fats
5. know your blood glucose levels by getting checked occasionally
6.watch out for Signs and symptoms of Diabetes eg feeling thirsty, losing weight, feeling vey hungry, feeling very tired and having blurry vision.

12/11/2023

Malingana ndi malamulo a dziko lino kufuna Kuzipha ndi Mlandu... Munthu amene Wafuna kuzipha akhoza kupezeka olakwa ku bwalo la milandu ndipo akhoza kukakhala kundende kwa dzaka mpakana ziwiri (section 229 of penal code).

Akatswiri ambiri azaumoyo amanena k*t lamulo limeneri silothandiza kweni kweni ponena k*t anthu amene amafuna kuzipha azilandira thandizo lakuchipatala mmalo mowapitisa kundende.

Lamuloli linayambisidwa mdziko muno nthaw ya ulamuliro wa atsamunda koma ngakhale dziko la Malawi likusungabe lamuloli, Ku Britain komwe ndikwawo kwa azungu omwe ankalamulira dziko lino Lamulo longa ili analithesa pano

Inu mk*tipo bwanj pachilamulochi.

Zimvere mumtolo😊
11/11/2023

Zimvere mumtolo😊

ADVERTISING

Malinga ndi kuchuluka kwa kubeledwa ndalama ndi akathyali ena pa nkhani zakapitidwe ka mmaiko akunja mnyamata uyu it's Heyss anayambitsa program yotchedwa 265chills imene amacheza ndi aMalawi omwe anapita kunja k*ti awaunikile aMalawi omwe amakhala ndi khumbo lozapita kunja monga iwo anachitila, program-yi imakhala loweluka lililonse nthawi ya six o'clock madzulo pa tsamba lake la Facebook lotchedwa It's Heyss. Lero ati wapeza nurse yemwe akufuna akawaunikile ma nurses anzake omwe amakhala ndi khumbo lozakagwila ntchito ku America, komanso wapeza akulu ena omwe anapeza ntchito ku Canada ndipo ali okonzekaso nawo kuphunzitsa aMalawi mmene iwo ntchito yawo anaipezela. Tiyeni amene tili ndi chidwi 6pm tikapezeke kumeneku.

It's Heyss

11/11/2023

Anthrax is a disease that can spread from animals to humans. You can get it by touching animals like cows, goats, or sheep that are sick. Eating meat from an infected animal can also make you sick.

Dont forget there is an outbreak of Anthrax in the neighbouring Zambia...let's also watch out and take preventive measur...
11/11/2023

Dont forget there is an outbreak of Anthrax in the neighbouring Zambia...let's also watch out and take preventive measures including avoiding eating meat that we dont realy know where it is coming from.
Report all suspected cases to your nearest health facilities.

Prevention is better than cure .

10/11/2023

Welcome ladies and gentlemen, boys and girls..😊
Takulandirani mabwana ndi madona, anyamata komanso atsikana😊
Tamupokelerani mose kose kose...

Address

Lilongwe Area 6

Telephone

+265997246220

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Vujah The Community Health Nurse posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share