12/10/2025
Pomwe tili Ku nyengo ya mother's day promotion
Shirt ya zachilengedwe herbals ili pa K6,500 yokha basi Koma ogula ma herb opitirira K60,000 akulandira shirt yaulere yokongola yobweretsa mwayiyi
Omwenso Ali ma top fan Ku Facebook akulandiranso shirt yaulere
Kuphatikiza apo, tikumatha kumuikira customer yemwe akugula Pafupi Pafupi ngakhale zomwe akugulazo pa nthawi yo sizikukwana K60,000
Awa Ali Ku NKHOTAKOTA ndipo apa agula C-4 ndi tseketseke sweet zomwe sizikukwana K60,000 Koma kamba koti agula mowirikiza/ Pafupifupi tawaikira shirt ya yellow ndipo alandira, ma suprise timathanso kupanga Kwa omwe akugula km tikutumiza kutali ( kutali wake tikunena Malawi muno osati kunja)
Mongokumbutsana, pa zachilengedwe herbals pano timathandizana ndi kutsatirana bwino polemba uthenga Ku WhatsApp 0886264833 osati kuimba foni or VN or SMS or Facebook ai choonde