24/07/2025
*KUTHAMANGA KWA MAGAZI (BP)*🫀
>Matenda awa ndi amodzi mwa matenda otchuka kwambiri amene akuvuta mmatupi wa anthu ochuluka. kudziwa zambiri za Bp kungakuthandizeni kudzisamalira moyenela ngati vutoli mukanalibe koma ngati labwela kale zingakuthandizeni kudziwa mmene mungathanirane ndi vutoli komaso kudzisamalira moyo wanu.
>Vuto ili limakhudza mtima ndi njira zodutsa magazi, kapopedwe ka magazi ku mtima ndi kayendedwe ka magazi kosayenela munjira zawo ndizimodzi mwa zifukwa zambiri zimene zimadzetsa vutoli.
🫀Mulingo osonyeza kuti BP ya munthu ilibwino umayenela ukhale 120/80mmHg kutsika mmusi, pamene ikaposa apa kumayambira cha ma 130+/80+mmHg kumakhala kuti uli ndi vutoli...... Pa pic pali zaka za munthu ndi momwe bp yake ikuyenera kukhalira
*ZOYAMBITSA*
0886264833
-kutengela ku mtundu
-kuchuluka kwa zaka 40yrs+
-Kunenepa
-kusapanga masewelo olimbitsa thupi
-zakudya za mchere or sugar kwambiri
-nkhawa
-zotsatira za mankhwala ena amene munthu ukumwa kwa nthawi Yaitali monga Arvs
-kukhala ndi pakati
-matenda a impsyo
-matenda a sugar ndi Zina zambiri.
🫀Bp imapangitsa kuti mtima uzigwira ntchito yopopa magazi ndi mphamvu kwambiri kuposera mmene zimayenela kukhalira zimene zimakhala zikubweretsa chiopsezo ku matenda ena a mtima monga kusiya kugwira ntchito, kutupa , kupanga madzi or kubooka kumene
>Kunenepa, kusapanga ma exercise ndi kudya mosasamala za thupi Maka za ma chemical, zamafuta, zamchere ndi za sugar, kumakolezela vutoli. Mafuta oipa amadzazana munjira zodutsa magazi choncho kayendedwe ka magazi kamakhala kovuta zimene zimatha kubweretsa vuto la stroke ngati mtsempha waphulika or watsekeka opita ku ubongo, ena ukaphulira amatha kukomoka pomwe ena anamwalira pompo. Mukachita mwai munthu amakhala bwino km mau amakhala asiya kuyankhula, ena mbali ina ya ziwalo imasiya kugwira ntchito zomwe zimavuta komanso Kutenga nthawi kuti achire.
>Zinthu zinaso zimathandizira kuti mitsempha ichepe (shrink) zimene zimakhala zikuika moyo wa munthu pa chiopsezo, Mk