09/07/2022
Ndipo mankhwala awawa palibenso maka C24/7...i had ovarian cyst ine in 2018-2019,and kuchipatala was told kuti zizakhala zovutilapo to conceive since cyst yo yapanga block chanichani kaya uko azachipatala zawozo...and was given microganon kuti ati amasungunula kaya but to no avail ..ndikamapita ku checkup amangondiuza kuti chikukulilabe chikapitilira they wu have to operate me...then someone introduced me to these mankhwala ..nnauzidwa ndigule a mwezi onse was taking 1,1,1 mmawa ,masana,madzulo...patatha mwezi went back to the hospital for checkup,behold, I was told am cyst free..ndipo even the doctor amene ankandipanga treat yo anadabwa kuti zakhala bwanji....a month later I was pregnant ,ndikunena pano uyu baby boy wanga akundimva apapayu will be turning 2yrs this coming August....as for me I can recommend kuti amene ali ndi vuto longa nnali nalo ine ayese C24/7 zichite kukanika zokha mutayesa rather than kukhalilatu..koma na kwa ine it worked 100%.