08/05/2025
Greetings All
Amtondo has organized a set of trainings in entrepreneurship.
A. Kodi mungapange business yanji malingana ndi :
1. Mpamba
2. Malo
3. Experience
4. Nzeru
5. Nyengo/weather
Other factors
B. Kodi mungatukule bwanji business yanu ?
Cholinga ndikuthandiza income generation
1. Omwe Ali pantchito kupeza njira zoonjezera zopeza chuma komanso kukonzekera retirement
2. Ana omwe akungokhala kumakukako kusowa zochita/poyambira
3. Housewives kuti athandizire income ya pakhomo.
4. Omwe Ali Kale ndi business koma sikutukuka malingana ndi Khumbo lawo
Venue: Likuni Hospital
Time: 2:00pm
Date: Friday 9 May 2025
Zofunikira
1. polemba and pen
MZAULELE FIKANI OSAOPA
For inquiries and bookings inbox
Timafika kuli konseko