SIikono Michael Usi

SIikono Michael Usi Contact information, map and directions, contact form, opening hours, services, ratings, photos, videos and announcements from SIikono Michael Usi, AIDS Resource Center, Sikousi@gmail. com, Nyambadwe.

what a man
11/10/2025

what a man

what's yo thought on this one
11/10/2025

what's yo thought on this one

Bambo Anga omwe ndi Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi ati ndiokonzeka kupeleka mpando komanso mphamvu...
24/09/2025

Bambo Anga omwe ndi Wachiwiri kwa mtsogoleri wa dziko lino a Michael Usi ati ndiokonzeka kupeleka mpando komanso mphamvu za ofesiyi kwa a Jane Ansah omwe apambana ndi a Peter Mutharika pa chisankho.

Malinga ndi chikalata chomwe a Usi alemba ndikusainira, panopa ndi zachidziwikire kuti a Mutharika apambana pa chisankhochi potengera mavoti omwe Amalawi awapatsa pa zotsatira zomwe Mec yatsimikiza kufikira pano.

A Usi ati Amalawi alankhura ndipo iwo alemekeza zokhumba za Amalawi.

Kotero iwo afunira mafuno abwino a Mutharika ndi a Ansah ndipo awapempha kuti atumikire Amalawi powapatsa ulamuliro wabwino.

A Usi amapikisana nawo pa chisankhochi kudzera pa tiketi ya chipani chawo cha Odya Zake Alibe Mlandu.

Wolemba:

22/09/2025

odya zake alibe mulandu

20/06/2024

Please help me to congratulate my Dad Mr Michael Manganya Usi for being chosen as a new Vice president of the republic of Malawi

Address

Sikousi@gmail. Com
Nyambadwe

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when SIikono Michael Usi posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram