07/03/2025
SAD NEWS ðŸ˜ðŸ˜
Kwachitika ngozi yoopsa pa Mr Chimwala a aang'ono pafupi ndi new apostolic church. Galimoto ya Trade ena amati Tedi/Thedi linanyamula azimayi agulu la m'mudzi mwa Lolo kupita kumaliro. Galimoto inawavundikira itagubuduzika. And azimayi awiri amwalira pomwepo awiri ena kuchipata ena avulala modetsa nkhawa. Tiyeni tiwaikize mma pemphero.