22/05/2026
Zizindingikilo 5 za mano zomwe mukufunika mukumane ndi Dentist nsanga nsanga
1. Kupweteka Kwa Dzino kuja komati liyamba lokha kenako lisiya lokha.
2. kutuluka magazi munkhama mukamatsuka mano
3. kutulutsa fungo nkamwa komwe sikumasiilapo
4. Sensitivity mukamwa zozizila pena zotentha
5. kutuma Kwa nkhama or nkhama zozungulila dzino
Dental Awareness is free