MWANA WA AMAMA flowrence

MWANA WA AMAMA flowrence Buying - selling

01/04/2022
20/09/2021

*UBWINO WA COLGATE*

1. *kuwalitsa nkhope yanu ndikuchosa ziphuphu kunkhope*

✍ phatikizani colgate ndi vasseline mkupaka ku nkhope kwanu then kudikira kwa 20 minutes kenako kutsukusulako ndi madzi otentha, izi muzipanga daily mpaka mutakhutira ndi maonekedwe a nkhope yanu.

2. *Kukunga mabere anu kuti aoneke ngati akamwana ka school* 🏫

✍🏻 sinjani Nkhaka Ndipo phatikizani zosinjidwazo ndi colgate mkupaka mabere anu kenako kutirani maberewo ndi masamba a cabbage then mkuvala bra wanu kwa 30 minutes then mkutsuka ndi madzi otentha, Pangani Izi Kawiri Patsiku mpaka mutawona kuti apa mabere anu ali njooo ngati makutu agwape.

3. *kuchotsa makanda ntchembere*

✍ sakanizani colgate ndi madzi amandimu mkumapaka Momwe muli makanda ntchemberemo then mkuzisiya choncho kwa 30 minutes then mkusuka ndi madzi otentha, pangani izi kawiri Patsiku mpaka makanda ntchemberewo atatha.

4. *Kuyeretsa mano*

✍ Sakanizani colgate ndi backing soda mkumakwechera mmano anu, Ndipo mano anu adzayera modabwitsa.

*"CHIZUNGULIRE"*_____________________________Health Counsellor;_*Dr. TIMOTHY K.👨🏻‍💻Online*https:/chat.whatsapp.com/FLOvB...
19/09/2021

*"CHIZUNGULIRE"*

____________________________

_Health Counsellor;_
*Dr. TIMOTHY K.👨🏻‍💻Online*
https:/chat.whatsapp.com/FLOvBH5GTxJHXgGz1F39qf
____________________________

👉 Ngati tawona kuti tikumapanga chizungulire koma mwakuti sitikudwala, tikuyenera kuganizapo mokwanira chifukwa chizungulire sichimangobwela mwachokha ayi.

*CHIMENE CHIMAYAMBITSA MATENDA A CHIZUNGULIRE*
👉 Kudwala mutu (litsipa).
👉 Kuchepa kwa magazi munthupi.
👉 Kudwala BP
👉 Kuganiza kwambiri
👉 Kukhala ndinkhawa
👉 Kusadya mokwanira (njala).
👉 Kutsegula m'mimba mowilikiza mumakhala mukutaya madzi ochuluka komaso mphamvu.

*MUNTHU AKAMADWALA CHIZUNGULIRE AMAKUMANA NDIZINTHU MONGA👇*
👉 Kusowekela mphamvu zamayimidwe komaso poyenda.
👉 Kumawodzela pafupifupi.
👉 Kumawona m'dima
👉 Kumawona ngati zilubwelubwe.
👉 Yekha kumadzidabwa kumakhala ngati wakomoka.
👉 Kusachedwa kuyiwala akayimilira malo amodzi kenako ndi kumakhala ngati akufuna kugwa
👉 Amava kwambiri ulesi

*ZOYENERA KUPANGA KUTI TIPEWE KAPENA KUTHETSA VUTO LA CHIZINGULIRE*

👉Muzimwa madzi okwanira osachepera 3 litres pa tsiku.
👉Muzidya zipatso zamitundu yosiyana siyana
👉 Kuwilitsa chidede ndikumamwa
👉 Kuwilitsa masamba yamtengo wapeyala ndikumamwa madzi akewo.
👉 Kuwilitsa njele zamtengo wapeyala ndikumamwa madzi akewo.
👉 Muchepetse Kuganiza kwambiri.

WhatsApp Group Invite

17/09/2021

*ZACHILENGEDWE*

*Zachilengedwe special*

*Mfiti*
~Mfiti zikuvutisa pakhomo pezani mtengo otchedwa cheteku mutenge zobala zake musinje muzifukiza mnyumba mwanu kawili olo katatu pa sabata mfiti siingasewereremo mnyumba mwanu,ngati cheteko watalikira pezani mchere muike mmakapu agalasi muike mmakona onse achipinda chanu kapena anyumba yanu mchere umatulusa positive power(mphanvu yabwino)
Mkukakoka mphanvu yoipa(negative power)mkuisokoneza

*KUMUPATSA TSOKA ONYADA*
•madzi amaliro
•mtuvituvi
Kumuthilira mmadzi osamba, olo wachuma chuma chimatha.

*KUBWEZA WACHIKONDI*
•mtengo/chingwe chomwe munthu anazimangilirapo
•tsamba la kamvuluvulu
•ndilire
•nthula
Kupanga ndudu musute kufukiza mnyumba komaso kukasamba mukunenelera.
_omwe zakuvutani kupeza bwerani ku inbox ndikuuzeni zochita zina zosavuta kupeza_

*MUKUFUNA KUTI MZANU AMENE MWAGONA NAYE MPHASA UMODZI AZIBWEBWETA ZOMWE WACHITA MASANA ONSE?*
~Ngakhale kuti anthu ambiri amasakaniza mitengo yambiri pa nkhaniyo koma mankhwala amene ali ofunika kwambili ndi awiri basi

~Mitengo iwili yokweshana koma imalila
mutsinje musakanize ndi chikasu
Mupange kathumwa muike ku pilo wa mzanuyo basi mugone,nthawi ikakwana kuti mankhwala agwile ntchito inuyo mudzuka chakudzusani simuchidziwa koma mukangodzuka mumva mzanuyo wayamba kulankhula zonse wachita masana inu m***a kumutepa zolankhulazo koma iye sadziwa kuti amalankhula.

*AKAZI AKUKUNANI?*
~Tsoka likakula ndi choncho

_Pezani mtengo wa mkotabwino muike mkamwa mumufunsire mkaziyo avomera._
*Omwe zikukuvutanibe bwerani ku inbox ndikuuzeni zochita Zina*

*MUKUFUNA KULIMBITSA CHIKONDI NDI MANKHWALA?*

*Zofunika*
~madzi apamwala

~Mitima ya nkhunda ziwili

~Chisoni chá mtengo ena amati fumbato

~Mulimbiko ena amati kondaine

*Kapangidwe kake*
~Muyanike mitimayo musinje yapange ufa musakanize ndi zinazo muike ku chakudya adye mmmmmmm muziyenda ngati ngumbi kulikonse muli limodzi.

17/09/2021

*NKHONDO KUNO AGOGO TADZAONAN ANA AJA KUNO AZIMAI AKUCHEPETSA NDATA PAMENE AZIBAMBO AKUKUZA GADAFI* *ANA APWETEKANA AWA* 😭😭😭😭😭😭😭😭

*KUCHEPETSA NDATA NDI KUKUZA CHIDA CHA ABAMBO*

Mupeze tsamba LA aloevera lathanzi bwino, mudure about 5cm or 6cm musende kuchoysa ka green outer layer both sides kuti mutsale ndikamkati kamaoneka ka transparent.

Kameneko mukatenge ndikumalowetsa kundatako every evening, leave it there till morning and do this for 10 days.

Ngati mungamachite mantha kuti kakhoza kulowa kwambiri NDE muzikaboola ndikumangilira kachingwe kuti mammawa muzingokoka kachingweko.

*KUKUZA GADAFI*

Mupeze aloevera wathanzi bwino about 6cm musendenso ka green outer layer both sides then muzipala kankatiko pang'onopang'ono kuti muzipanga ka thin paste then add 1 teaspoon glycerine and one vitamin E capsule. Mix them together thoughly mpaka ziphatikizane bwino.
Tengani mixture iyi nkumapanga massage GADAFI or auzeni akondedwa any azikuthandizani kupanga massage GADAFI yo. Do this morning and evening for several days

*KUONJEZERA MPHANVU AZIBAMBO*

zofunika
Egg
Lemon
Natural honey

Zoyenera kupanga
Phwanyirani dzila mu bowl, mukatero muchotsemo yoke chifukwa Ife tikufuna egg white yokha.
Dulani ndimu lamu pakati ndipo finyirani mu dzilamo, kwa omwe simungakwanitse kumwa chifukwa cha funfo ladzila mukhoza kufinyira both sides of the lemon

Add 2 table spoons of natural honey.

Mukatero imwani mixture iyi kawiri patsiku mammawa on empty stomach and madzulo in the evening before

17/09/2021

🤰🏻Labour pain =ngati mukufuna kuchepetsa labour pain(ululu omwe mai amanva pobeleka)mudzimwa tea wa mkandamkhuku pafupipafupi
🍃ZIPYELA=kuchotsa zipyela sakanizani ufa wa mthangala za mpiru ndi uchi ndipo pakani pamalopo kufikila zipyela zitachoka zimachoka ndithu
💐KUFOOKA KWA THUPI=Viikani mitsitsi ya nthochi mmadzi okwanila 1ltr gawani patatu ndi kumwa
🍋KUSANZA MAGAZI=idyani Nthochi yophika Pafupi pafupi,3x a day
kwa 1wk
🧅KUSADWALADWALA=Mudzidya masamba amalambe monga ndiwo or kuika ufa wamasamba amalambe mundiwo zanu or kuwilitsa masambawo mkumwa ngati tea osaika sugar m***a kuika uchi ngati ulipo

17/09/2021

*KUONTCHA KWA MAPAZI*

👉 Vuto lakuotcha mapazi limakonda kuchitika kwa munthu oti amakonda kungokhala mwakuti akayenda wayenda pagalimoto kapena kukwezedwa njinga komaso maka anthu onenepa.
👉 Vutoliso limatha kuyamba ngati munthu sakudya zakudya zamagulu.
👉 Penaso zimakhala zizindikiro za matenda monga bp, shunga ndi zina.

*"NJIRA ZA CHILENGEDWE ZOTHANA NDI VUTO LA KUONTCHA KWA MAPAZI"*

*1). "Pezani Apple Cider Vinegar."*
👉 Muzitenga thonje kapena kasalu kumakanyowesa menemo ndikuma thowela mapazi anuwo katatu patsiku.

*2). "Pezani mchere wa Epson"*
– Kuthira mchere wa Epsom m'madzi odzadza ka beseni kakang'ono koma kakuti mapazi anu akhoza kulowamo, ndikuviyikamo mapadzi anuwo kwa 15 minutes.

*3). "Pezani kholowa."*
– Kumusinja kumanga mukasalu madzi akewo kuwafinya mkupanga mapazi anuwo.

*4 ). Pakanimo Colgate.*

*5). Pakani mapazi anuwo ma slice tomato🍅.*

*6). "Mupeze ma beseni awiri"*
–Inayo mudzadzemo ndimadzi ozizira. Inayo mudzadzemo ndimadzi otentha.
– Muyike mapazi anu mubesi lamadzi otentha akhalemo kwa 3 minutes, mukangochotsa pompopompo muyike mapaziwo mu beseni lamadzi ozizira akhalemo kwa 5 minutes kenako muyikeso mapaziwo m'beseni lina lija.
Muzingobwerezabwereza.
– Kumapanga kawiri pa tsiku

*"( Munali ndine Caren wa NYUMBA YAMACHILITSO WHATSAPP GROUPS +265995629944 )"*

06/09/2021

*CONJUNCTIVITIS*

*MASO A MANTHONGO*



*🌱Kutuluka manthongo mmaso ndi nthenda yomwe imagwila aliyense mwa or Mkulu ndipo imayamba kamba kazifukwa zingapo, monga Madzi omwe timamwa, michere ya pathu ija yomwe imatuluka ndi thukuta ndizina zambiri.*

*ZIZINDIKIRO ZOCHEPA*

```〽️Odwala amamva kuontcha mmaso akaima madzuwa.```

```〽️Maso amafira```

```〽️Kusaonesesa```

```〽️Misonzi imangogwa yokha ndizina zambiri.```

*NJIRA ZACHILENGEDWE*

*1. INDIAN GOOSEBERRY*

```〽️Ngati mwavutika ndimaso a manthongo muzitenga 1 Cup gooseberry juice mutasakaniza 2 teaspoons uchi mkumamwa kawiri pa tsiku.```

2. *CORIANDER SEEDS*

```〽️uziwiritsa 1 tea spoon coriander seed mu madzi okwana glass imodzi kwa mphindi zokwana khumi ndizisanu ndikuwadikila apole wezi ndikumatsukira mmaso mwanu.```

3. *TURMERIC*

〽️ ```Thilani 1 teaspoon tumeric mmadzi okwana glass imodzi mkutakasa. Mukatero tengani ka towel ndikuviika mmenemo ndikuvuula. Kenako siyani kaume ndikumapukutila mmaso mwanu kawiri or katatu patsiku.```

4. *GOLDEN SEAL*

*```〽️Muzithila 1 teaspoon ya golden seal mu glass ya madzi omwe mwawawiritsa. Zisiyeni kwa phindi 15 kenako m***a kumasukila madziwo diso lokhuzidwa.```

*NGATI MANTHONGO ATULUKA KWAMWANA*

```🌱Ngati vutoli lagwa kwa mwana njira ndi iyi ⤵️```

*MKAKA WAM'MAWELE*

```〽️Muzimudothesela mwanayo mkaka wanu wammawele ndipo vutoli limatha mosavuta.```

*OSAYIWALA KUWAGAWIRA AZANU MWA ULELE*

06/09/2021

*Dr KHUDZE WA LET HERBS CURE ME*

*"KODI GONDOLOSI ANGATITHANDIZE BWANJI?"*

👉 Gondolosi titha kugwirisa ntchito ngati tili ndi likodzo
👉 Ngati tili ndi nyongolosi za m'mimba tisadandaule, tipeze Gondolosi tizimwa.
👉 Kwa amene tinakaponda posakhala bwino ndiye tatenga Chindoko, tithamangire pamene pali Gondolosi tizimwa
👉 Ngati zakudya sizikugaika m'mimbamo kapena tadzimbidwa tipeze Gondolosi timwe kapena kutafuna
👉 Ngati Asthma imativuta tiyang'ane komwe kuli Gondolosi tizimwa
👉 Kwa amuna amene tikufooka kuchipinda, tisadandaule tipeze Gondolosi tizitafuna kapena kumwa
👉 Kwa azimayi omwe akuyamwisa ngati mkaka sukutuluka m'mawere, apeze Gondolosi azitafuna kapena kumwa
👉 Ngati azimayi timavutika kwambiri pobereka tizikonda kutafuna kapena kumwa Gondolosi
👉 Kuti mamuna kapena mkazi akhale ndi chilakolako chogonana akuyenera akhale ndi "Testolene hormones" okwanila mthupi, choncho ngati chilakolako simukhala nacho muzikonda kutafuna kapena kumwa Gondolosi
👉 Ena sitikhala ndi chilakolako cha zakudya, tiyeni tipeze Gondolosi tizitafuna kapena kumamwa
👉 Ngati m'mimba mumakuvutani, musade nkhawa, pezani Gondolosi muzitafuna kapena kumamwa.

*"( Munali ndine Dr KHUDZE WA LET HERBS CURE ME +265995577730*

02/09/2021

*LET HERBS CURE ME BY DR KHUDZE* Dr KHUDZE +265998562094)

*"KUIPA KWA CHIZOLOWEZI CHODYA DOTHI."*

👉 Pali anthu ena pazifukwa zovuta kumvetsa amakhala ndi chizolowezi chodya dothi. Mwakuti ngati sadya dothi mtima wawo sukhala mmalo ndipo imakhala ngati "addiction" (chinthu chovuta kusiya)
👉 Kudya dothi ndi vuto limodzi mwa mavuto omwe azachipatala timati PICA lomwe ndi vuto lomwe munthu amakhala ndi chikhumbokhumbo chodya zinthu zopanda ubwino wake weniweni kapena thanzi lililonse kuthipi monga kudya ice, dothi ndi zina.
👉 Nthawi zambiri achipatala timati ndi vuto la mu ubongo komanso kusintha kwa zinthu zina mthupi la munthu mwachitsanzo mayi akakhala oyembekezera.
👉 Kwa ena limakhala khalidwe la kwawo (culture) komanso ena chifukwa cha njala.

*"KODI KUIPA KWAKE PA UMOYO WA ANTHU NDIOTANI?"*
👉 Kudya dothi kumapangitsa kuti michere ina yomwe timaipeza mu zakudya isatengedwe bwino kupita mmagazi. Mwachitsanzo mchere wa Iron omwe umathandiza popanga magazi sumatengedwa bwino ndipo zimatha kupangitsa munthu kudwala nthenda yosowa magazi.
👉 Palinso matenda ena monga mitsempha kukanika kugwira bwino ntchito yake.
👉 Komaso pomwe mukudya dothi m'mimba mumakhala nyumba ya njoka za m'mimba ndi tizilombo tina tomwe timapeza malo ochulukirana. Njoka za mmimba zimatha kupangitsa matenda osiyanasiyana.
👉 Kudya dothi kumatha kuyambitsa vuto la kusowa kwa chilakolako cha chakudya komanso ena akadya dothi lambiri kukhuta kumakhala komweko kupangitsa kukanika kudya zakudya zofunikira.
👉 Pamene muli oyembekezera nkumadya dothi mumatha kubweretsa vuto la kusowa kwa magazi kumaika chiopsezo pa moyo wanu ndi wa mwana wanu osabadwa kotero nkofunika kupewa kutero.
👉 Matenda a blood pressure (BP) komaso nthenda yamtima imayambaso chifukwa cha chizolowezi chodya dothi.

*"TINGASIYE BWANJI KUDYA DOTHI?"*
👉 Vuto lodya dothi limakhala chizolowezi chovuta kusiya. Zimafunika khama la mwini wake komanso kupempha chithandizo kwa amzanu.
👉 Ena amayesesa kupeza zinthu za zokoma za "

18/08/2021

*CLINIX HEALTHY GROUP*🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊🍊

*UBWINO OKONDA KUDYA MA ORANGE*

```🍊Ma orange ndichakudya chabwino kudya chifukwa muli zinthu zambili zomwe ndizofunika kuthanzi lathupi lathu```

```Ngakhale kuti ambili timakonda kudya ma orange koma sitidziwa ubwino omwe umapezeka muma orange```

*🥦UBWINO WA ORANGE🍋*

```↪ Orange imamupangisa munthu kukhala ndi thupi losalala kotelo kuti chiphuphu sichimaka paiye```

```↪ Orange limapangisa kuti chitetezo chanthupi chikhale chokwanila kotelo matenda amavuta kukhala nthupi, komaso kwa omwe ali postive ndibwino kumadya kwambili ma orange```

```↪ Orange limathaso kuthandizila ntchito yakuchipinda ndipo abambo komaso amayi ngati mukumadya ma orange kwambili muzaona kusintha pakagwilidwe kantchito kuchipinda```

```↪ Orage limamupangisa munthu kukhala mu mood yabwino maka panthawi yomwe waona kuti wabalalika pachina chake inu ingotengani orange mudye muzakhala bwino```

```↪ Mu orange muli vitamin c yemwe amakhala ofunikaso kwambili ku mano anthu choncho kudya ma orange ambili mano anu azakhala olimba```

```↪ Mukamadya ma orange simuzakhala ndi vuto lamaso chifukwa orange limapangisa kuti maso athu aziona bwino ndikuwateteza kumatenda osiyana siyana```

```↪ Ma orange amathandiza kuti ma cells acancer asachuluke mthupi```

```↪ Ma orange amathandizila kugaya chokudya nthupi choncho mukamaliza kudya ndibwino kudya orange kuti digetion izichitika bwino```

```↪Ma orange amathandiza ntima maka pakayendedwe kamagazi komaso amachepesa mafuta nthupi```

```↪ Amathandizaso kuti tsisi lizikhala lokuda bwino komaso silidukaduka```

```↪Ngati muli ndi vuto la asima yambani lelo kukonda kudya maorange muzachila mosavuta``

*CLINIX HEALTHY GROUP*

Address

Fissantekraal
Cape Town

Opening Hours

Monday 09:00 - 17:00
Tuesday 09:00 - 17:00
Wednesday 09:00 - 17:00
Thursday 09:00 - 17:00

Telephone

+27640340113

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when MWANA WA AMAMA flowrence posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Contact The Practice

Send a message to MWANA WA AMAMA flowrence:

Share

Share on Facebook Share on Twitter Share on LinkedIn
Share on Pinterest Share on Reddit Share via Email
Share on WhatsApp Share on Instagram Share on Telegram

Category